19/08/2026
Nyungwe FM Sports
Mayi wa fuko lino Gertrude Mutharika wafika pa bwalo la ndenge la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe komwe atsogolere kulandira timu ya Scorchers pa ulendo wake ochokera ku mpikisano wa WAFCON komwe inathera pa nambala yachiwiri.
Ku bwalori kwafikanso anthu osiyanasiyana okonda mpira kuphatikizapo nduna yowona za masewero Alfred Gangata ndi nduna zina zochuluka.
Timuyi ikuyembekezereka kufika nthawi ya 15:30.
Wolemba : Robert malenga