Big Trump

Big Trump Malawian (Artist | Producer) from Blantyre at NB Recordz πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ“€πŸŽ§
For Bookings πŸ“²: +265 988 739 969

Mwaona??πŸŽ™οΈπŸŽ§πŸŽΆBlack Nina   πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ“
03/09/2026

Mwaona??πŸŽ™οΈπŸŽ§πŸŽΆ
Black Nina

πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ“

Producer Wa Malawi Mastyle America...πŸ‘‘πŸͺ˜πŸ”₯
01/09/2026

Producer Wa Malawi Mastyle America...πŸ‘‘πŸͺ˜πŸ”₯

30/08/2026

Ichi mpaka chaka cha mawa chikubangula πŸ”₯πŸš¨πŸ“ Prod by yours Big Man Trump πŸ˜Ήβœ…
Contact us - 0988739969

Mugone Bho..πŸ€²βœ”οΈ
28/08/2026

Mugone Bho..πŸ€²βœ”οΈ

21/08/2026

πŸŽ™οΈ KWA MA UPCOMING ARTISTS A KU MALAWI πŸ‡²πŸ‡Ό β€” PART 2

Ngati ndinu upcoming artist, musamaganize kuti nyimbo iliyonse yomwe mwajambula iyenera kutulutsidwa. ❌🎢

Nthawi zina muli ndi nyimbo 10, koma mwina imodzi kapena ziwiri zokha ndi zomwe zingakuyimireni bwino.

Musanatulutse song, dzifunseni:

πŸ”₯ Kodi nyimboyi ikundiyimira ngati artist?
🎧 Kodi sound yake ndi yabwino mokwanira?
❀️ Kodi anthu angamve ndikufuna kuyimvanso?
πŸ“± Kodi ndili ndi plan ya promotion?
🎯 Kodi nyimboyi ili ndi cholinga, kapena ndikungofuna kungotulutsa?

Musamangotulutsa nyimbo chifukwa muli nayo. Tulutsani chifukwa ndi nyimbo yomwe mukukhulupirira kuti iyenera kumveka.

Kumbukirani kuti quality + identity + consistency zingakuthandizeni kupita kutali kuposa kungotulutsa ma song ambiri opanda direction.

Upcoming artist, nyimbo yako yotsatira ikhoza kukhala yomwe anthu akhala akuyembekezera. πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ”₯

Kodi inu mumakhala ndi nyimbo zingati zomwe simunatulutse chifukwa munaona kuti sizinakwanire? πŸ‘‡πŸ½

20/08/2026

πŸŽ™οΈ KWA MA UPCOMING ARTISTS A KU MALAWI πŸ‡²πŸ‡Ό

Ngati ndinu upcoming artist, chonde musamangofuna kutchuka mwachangu. Yambani ndi kumanga artist amene anthu adzafune kumudziwa kwa nthawi yayitali. ❀️‍πŸ”₯

Musamangothamangira studio chifukwa mukufuna kungotulutsa nyimbo. Phunzirani kulemba nyimbo, konzani ma vocals anu, dziwani mtundu wa music womwe mukufuna kupanga ndipo pezani producer amene akumvetsa direction yanu. 🎢

πŸ’‘ Muzisankha anthu omwe mukugwira nawo ntchito mosamala. Sikuti munthu aliyense amene ali ndi studio, camera kapena ma followers ambiri ndiye munthu woyenera pa career yanu.

🀝 Pangani ma connection abwino. Lemekezani ma producer, artists anzanu, DJs, videographers, photographers ndi anthu ena omwe ali mu industry. Music industry imamangidwa ndi ma relationships.

πŸ“± Muzigwiritsa ntchito social media mwanzeru. Musamangopost nyimbo yanu yokha. Sonyezani anthu who you are, ntchito yanu, ma behind-the-scenes komanso zomwe mumakhulupirira ngati artist.

πŸ’° Ndipo chonde, phunzirani kuyika ndalama mu career yanu. Beat yabwino, recording yabwino, artwork yabwino, video yabwino komanso promotion zonse ndi investment. Koma musamangowononga ndalama chifukwa munthu wina wakuuza kuti β€œizi zikupangitsa kukhala star.”

πŸ”₯ Consistency is everything. Nyimbo imodzi ikalephera sikutanthauza kuti career yanu yatha. Phunzirani pa mistake, bwezerani mphamvu ndipo pitirizani.

Ndikufuna kuona ma upcoming artists ambiri aku Malawi akukula bwino komanso akupanga zinthu zomwe tingadzinyadire nazo. πŸ‡²πŸ‡Όβ€οΈ

Musamangofuna kukhala famous. Fufuzani kukhala GOOD, kukhala UNIQUE komanso kukhala CONSISTENT.

β€” Big Trump πŸŽ§πŸŽ™οΈ

πŸ”₯🎹 MA ARTIST, THIS ONE IS FOR YOU! 🎧πŸ”₯Ndatsegula WhatsApp Group yapadera ya ma BEATS 🎢Kumeneko ndiziponyamo ma beat atsop...
18/08/2026

πŸ”₯🎹 MA ARTIST, THIS ONE IS FOR YOU! 🎧πŸ”₯

Ndatsegula WhatsApp Group yapadera ya ma BEATS 🎢

Kumeneko ndiziponyamo ma beat atsopano omwe ma artist angagule ndikugwiritsa ntchito pa nyimbo zawo. πŸ’―πŸ”₯

🎡 Afrobeat
🎡 Hip Hop
🎡 Dancehall
🎡 Trap
🎡 Drill
🎡 R&B
🎡 Afro Pop
🎡 Afro Fusion
…ndi ma style ena ambiri.

Ma beat abwino, ma sound atsopano komanso ma beat osiyanasiyana pa artist aliyense. πŸͺ˜βœ”️

Ngati ndinu Artist ndipo mukufuna kupeza ma beat atsopano nthawi zonse, JOIN THE GROUP.

πŸ“²(+265 988 739 969) Mukufuna kulowa? Nditumizireni DM ndikupatseni link....πŸ€πŸ’―πŸ”₯

17/08/2026

Achina G A
Srs business (0988739969)

Kuno ndikomwe timapanga SOUND. 🎧πŸ”₯Recording | Beat Production | Mixing & MasteringArtist aliyense amene akufuna kukweza l...
17/08/2026

Kuno ndikomwe timapanga SOUND. 🎧πŸ”₯

Recording | Beat Production | Mixing & Mastering
Artist aliyense amene akufuna kukweza level yake, tili ready.
πŸ“ Ngumbe, Chileka
πŸ“² Book your session with Big Trump
(0988739969)

Another session. Another sound.We don't just record music β€” we build the sound. 🎧πŸ”₯πŸŽ™οΈ Recording🎹 Beat Production🎧 Mixing ...
16/08/2026

Another session. Another sound.
We don't just record music β€” we build the sound. 🎧πŸ”₯
πŸŽ™οΈ Recording
🎹 Beat Production
🎧 Mixing & Mastering
πŸ“ Ngumbe, Chileka
πŸ“² Book your session with Big Trump

Address

Chileka

Telephone

+265983907336

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Big Trump posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category