MFDtv and radio

MFDtv and radio Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from MFDtv and radio, Radio Station, Chilinde.

17/04/2026

Good morning people

15/04/2026

ZOMVETSA CHISONI 💔

Apolisi m'boma la Kasungu atsimikiza kuti a Bonfance Kachamba ndiwomwe amwalira pa ngozi yomwe yachitika lero mu msewu wa M 18 Kasungu-Nkhotakota pa mphambano yopita ku Kamuzu Academy ku Mtunthama.

Izi ndi malinga ndi mneneri wa apolisi m'bomali a Joseph Kachikho.

A Kachamba anavulala kwambiri mmutu, mnzawo yemwe anali naye panjinga yamoto wavulala kwambiri mwendo ndipo anathamangira naye pa chipatala chachikulu cha Kasungu pomwe yemwe amayendetsa galimoto yomwe inaomba awiriwa ali pa njingayo Denis Moyo, wavulala koma osati modetsa nkhawa.

A Kachamba amachokera m'mudzi wa Maliwa mfumu yayikulu Chulu m'boma la Kasungu

Mzimu wawo uuse mu mtendere 🕊️🕊️

13/04/2026

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

13/04/2026
13/04/2026

🙏🙏🙏

Koma katunduyu muzatenga ndithu
06/02/2026

Koma katunduyu muzatenga ndithu

Address

Chilinde

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MFDtv and radio posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share