Udabwa

Udabwa Udabwa

Advertising agency

Udabwa WhatsApp number 0996 76 67 60
(1)

18/08/2026

‎Anati chan Alendo Atakanika Kutsekura Food Warmer🤣😂

18/08/2026

Tilipo angati amene tadzuka ndi moyo malo ano ? Wakufa sayamika

17/08/2026

ukangokwanisa zaka 25 kumapita kwinako sumatcheranso alarm amakudzutsa ndimavuto ako🤔

17/08/2026

Usiku uno KUMWAMBA kukumbukile mapemphelo Ako mawa kukamacha mu phone mwako ulandile good news

Koma Jay Jay Cee Mw uja ndi Dolo guysSamalimbana ndi alibe matukutukuUlemu wako fadah
17/08/2026

Koma Jay Jay Cee Mw uja ndi Dolo guys

Samalimbana ndi alibe matukutuku
Ulemu wako fadah

17/08/2026

MULUNGU amagwiritsa ntchito zonyozeka

Ngati ena amakuyang'anirani pansi adzaonanso mukukwezedwa 🙏

17/08/2026

Pa ogwira ntchito onse ndi mphunzitsi ekha amene amamenya ma customer ake
���

17/08/2026

Pa ukwati mukazapeza akuchikazi akuvina kwambrii
Ziwani kuti mwatenga wa mimba kale 🤦🤦😩

17/08/2026

Ngati Abraham anakwanitsa kupha Goriath, everything is possible

Never give up👍

17/08/2026

Azimayi, mwamuna wanu adayambapo wakuyamikirani ndikukuthokozani pazabwino zomwe mumamuchitira pamodzi ndi family yonse?

Address

Kawale 2
Chilinde

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Udabwa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share