CSJMalawi

CSJMalawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from CSJMalawi, Media/News Company, Plot 007, S146 Limbe-CZ Boma Road, Yasini Market, Chiradzulu.

Centre for Solutions Journalism (CSJ) is a human rights media organisation which uses the media, specialised training and key stakeholders' engagement in its advocacy work.

06/06/2026

Men's Guilds of various churches should assist men facing depression through counselling

06/06/2026

There is need for bar owners to be innovative. Let bars have social football and other social sporting teams.

06/06/2026

There is need for bar owners to be innovative. Let bars have social football and other social sporting teams.

06/06/2026

BODZA LALIKULU
Mwamuna salira. Mwamuna ndi munthu. Monga munthu aliyense amalira.

Malawi Electoral Commission (MEC) Chief Elections Officer, Andrew Mpesi, has resigned from his positionIt is not yet kno...
26/05/2026

Malawi Electoral Commission (MEC) Chief Elections Officer, Andrew Mpesi, has resigned from his position
It is not yet known why he has tendered his resignation.
His resignation comes after MEC has been tussling with the Executive following an order that the electoral body's head office should relocate to Blantyre.
MEC challenged the order in the courts

Kodi King Vuto awuza chiyani khoti lisanamupatse chigamulo? Kodi iye aoulumuka pa mlandu wogwililira Naliyera? Tiyeni ti...
26/05/2026

Kodi King Vuto awuza chiyani khoti lisanamupatse chigamulo? Kodi iye aoulumuka pa mlandu wogwililira Naliyera? Tiyeni timvere limodzi.

Lena amenya khoma Dr Tallina atakana kumuchotsa pakati atamuwuza ku...

SE2 Fupa Lokakamiza Episode 5Kodi ungapange bwanji kuti uteteze chibwenzi chako pamene maso ake akudyelera kwina? Zex al...
23/05/2026

SE2 Fupa Lokakamiza Episode 5
Kodi ungapange bwanji kuti uteteze chibwenzi chako pamene maso ake akudyelera kwina? Zex alangiza Tapiwa za chinsinsi cha chikondi. Tiyeni timvere limodzi?

Kodi bwenzi lako la pa mtima litadyelera maso ake kwa mtsikana kapena mayi wina ungapange chiyani kuti chikondi chanu chibwelere m'chimake? Zex apereka langi...

Fupa Lokakamiza li..........Komatu ziliko. Warrior akuti ma Rasta ali ndi 'mgonero' wawo umene amagwiritsa ntchito pa ma...
14/05/2026

Fupa Lokakamiza li..........

Komatu ziliko. Warrior akuti ma Rasta ali ndi 'mgonero' wawo umene amagwiritsa ntchito pa mapemphero. Kodi holy communion ya ma Rasta ndi chani? Tiyeni timvere limodzi.

Fupa Lokakamiza Season 2 Episode. Mayeso alandira laptop kuchokera kwa Tithan pamene Tapiwa wakwiya kwambiri ndipo walavula makala amoto kwa Zex. Mayi a Lind...

14/05/2026

Kumenya kapena kupha anthu powaganizira kuti amachita za ufiti ndi matsenga ndi kuphwanya malamulo. Mukachita zoterezi mumangidwa.

Address

Plot 007, S146 Limbe-CZ Boma Road, Yasini Market
Chiradzulu
306107

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CSJMalawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to CSJMalawi:

Share