RADIO Bembeke FM

RADIO Bembeke FM RADIO BEMBEKE FM is a community radio situated in Dedza which aims at helping people in this communi

19/05/2017

A few weeks ago we invited Kenneth Namalomba to be part of the Nyau art project and to our surprise he had already been working on his own…

01/01/2017

Happy new year to you all Radio Bembeke Family!!!!!
Be blessed in 2017

16/10/2016

Tsiku lija ndilelo tikukhazikitsa Radio Bembeke football league! !!!!!
Malo: Dedza stadium
Nthawi : 1:00 masana lero
Oimba : Nepman, sam simakweri
Bwerani nonse kuzapanga launch league yanu, league yathu! !!!!!!!!!

03/08/2016

RADIO BEMBEKE LERO YATHA CHAKA CHIMODZI !!!!!
ZIKOMO KWAMBIRI POKHALA NAFE KOMA PA KUTI PANGA SUPPORT. MULUNGU AKUDALISENI.

osaiwala pachiweru 6 August 2016, tili Ku stadium komwe tikapange masewera osiyanasiyana, monga football, netball, fishifishi, fulaye, tag of war, kudumpha mumasaka, ndi Ena ambiri

Pobwera bwerani mutavala zozasewerera mphoto nzosayamba
Bwerani nonse

03/08/2016

IT'S RADIO BEMBEKE'S 1ST BIRTHDAY!!!!!
WE THANK YOU ALL FOR SUPPORTING US
MAY GOD RICHLY BLESS YOU!!
SEND YOUR SHOUT OUTS AND CELEBRATE WITH US

Don't forget Saturday the 6th August we have a sports day at the stadium come in your sports attire!
Football, netball, tag of war, high jump, long jump, sack jump, and many more activities, with amazing prices

15/07/2016

Kuzizila nde kwazizila, koma tisaike mbaula yosanyeka mnyumba,
Utsi wambaula umapha.

25/05/2016

Wosewera mpira wa Dedza young soccer Edward Nsamala watisiya dzulo ndimabala omwe akukhulupililidwa kuti anali a bomba.
Thupi lamalemuyi likuikwidwa mmanda masana ano
Ause mumtendere Edward!!!

25/05/2016

Dedza football family mourns the death of Edward Nsamala who was a Dedza young soccer player.
He passed on from injuries from what is believes to be a gr***de bomb
He is being laid to rest this afternoon.
May his soul rest in peace.

22/05/2016

ComedianJohn Nyanga well know for his character as Izeki in Izeki ndi Jakobo or Prophet has passed away today.. Burial will be on Tuesday.. The country has lost an important Art figure and pioneer of democracy through his Art... We will forever miss Izeki

18/05/2016

Madzulo ano kuchokera 8 pm tikhala tikupitiliza kikambilana nkhani ya kukhulululilana mmabanja, komanso ma relationship a serious
Mu studio ndikhala ndi a bambo omwe tithandizane kuyankha mafunso any
Omwe mukhoza kutumiza p***a komanso pa 0881120037
Tiyeni tikhalile limodzi

11/05/2016

A Malawi anzanga tafika bwanji apapa pomapha munthu nzathu(albino) mkumati ndi business.
Chitetezo chawo chagona mmanja mwathu
Tiyeni tikondane.

11/05/2016

It is sad how as Malawians we have come to killing fellow humans (albinos) in the name of business
Let love lead, lets be our brothers keeper

Address

P. O. Box 18
Dedza

Telephone

+265111644526

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when RADIO Bembeke FM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share