Dwangwa Touch TV

Dwangwa Touch TV It's all about Informing, entertaining and educating. Dream Big
Emulate your dream
Change your life
Promo wap/call+265(0)889464089
(1)

Happy birthday kwa die-hard football fan!  Munthu amene anaonera ma game onse a FIFA World Cup 2026 kuyambira koyamba mp...
10/09/2026

Happy birthday kwa die-hard football fan! Munthu amene anaonera ma game onse a FIFA World Cup 2026 kuyambira koyamba mpaka komaliza! 😂🏆

Tithandizeni kumufunira tsiku lakubadwa lopambana 🥳

10/09/2026

Posatengera Budget yanu ndi sukulu iti ya Sec. muNkhotakota yomwe mungatumizeko Mwana wanu And Chifukwa Chani ? Ena amfunsa inbox

10/09/2026

Kodi chifukwa chani akazi ambiri amadana ndi amuna andalama?

Kuyionetsa Amayi akunyumba"Ndine "Dolo" ndinalandira mdulidwe wa Abambo wakuchipatala"
10/09/2026

Kuyionetsa Amayi akunyumba

"Ndine "Dolo" ndinalandira mdulidwe wa Abambo wakuchipatala"

10/09/2026

Ngati Kukongola Ndi Tchimo
Ambiri Pa Group Pano Ndinu Olungama. Good morning!!

Tomorrow's fixture. Ladies Football 8:30Factory vs Ten Rocks (Chitowe)Matiki 3  vs Bana (upper)Sugar star vs Ten Rocks (...
09/09/2026

Tomorrow's fixture. Ladies Football 8:30
Factory vs Ten Rocks (Chitowe)
Matiki 3 vs Bana (upper)

Sugar star vs Ten Rocks (Chitowe) 9:30
The Hunters vs pool(upper)

09/09/2026

Good night Babe ❤️, Inde Iweyo amene umangogona ngati Chiwetowe

09/09/2026

Ayi si Wakisa Poya (Face off) Zangofafana. Anthu apa Mudzi Pano ndinu opalamulitsa 😅

TO OUR FOLLOWERS Zatifika kuti anthu ena amaganiza kuti timangopanga ma post a anthu omwe timawadziwa kapena anzathu. Ko...
09/09/2026

TO OUR FOLLOWERS

Zatifika kuti anthu ena amaganiza kuti timangopanga ma post a anthu omwe timawadziwa kapena anzathu. Koma zoona zake ndi ayi. Ife timapanga post ya aliyense amene watifikira. ❤️

Birthday, Valentine kapena chikondwerero china chilichonse, timakondwera kukondwera nanu komanso kugawana chisangalalo chanu kwaulere.

Ngati ndinu Top Fan, ichi ndi chimodzi mwa zinthu zomwe Top Fan aliyense akuyenera kulandira mwaulere.Just hit us inbox.

Ndife banja limodzi, ndipo aliyense ndi wofunika kwa ife.

Court laletsa a Sameer Sulemani kukhazikitsa Commitee yoti iunikire za Katangale yemwe akuchitika mma Company a boma.A S...
09/09/2026

Court laletsa a Sameer Sulemani kukhazikitsa Commitee yoti iunikire za Katangale yemwe akuchitika mma Company a boma.

A Sulemani ananena mu Parliament kuti pali ma Company 12 aboma akukaikitsa kuti zinthu zawo sakuyendetsa bwino ndipo afufuzidwe koma lero Court lapereka Chiletso pa Ganizoli.

Address

Dwangwa

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dwangwa Touch TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Dwangwa Touch TV:

Shortcuts

Share

Category