New Politics Magazine NPM

New Politics Magazine NPM News and Current affairs

12/04/2023

Tune times radio imbani phone nkhani yake ya lero ndiya fodya basi phone yanu ndiyofunika kwambili!!🙌

07/01/2023

Rashley Mw tikudikira mwachidwi bundle tagula kale boss titsitse chinyimboyo👍

07/01/2023

Mwadzuka bwanji bwana Lucius Chiccio Banda ?koma munayankhula zongwila ntima kwambili mu Times Exclusive interview 🙏

07/01/2023

Mwadzuka bwanji kulikonse komwe muliko?

06/01/2023

Good night all🙏

06/01/2023

D.N.A TEST WATHETSA BANJA.

Mai wina mdziko muno manja ali nkhosi banja lake litatha kamba kachi machine chotvhedwa DNA test.

Nkhani yonse ikuti maiyu amamuzembera mamuna wake ndipo amapanga zadama ndi mwamunanwina wachibwezi mpaka anamupatsa pathupi koma mwamuna wake wanyumba samadziwa kalikonse ndipo amangoti mimbayo ndi yake mpaka mwana anabadwa koma mkuyamba kumulera bwino bwino ngati wake ndithu.

Koma poti mudziwa mwana wamamuna ndikabudula amathera moyenda mamunayu nyengo zake zinafika povuta moti mpaka anapita kwa sing'anga kukafuna mankhwala oti alemere kuti nyengo zake zisithe koma akuti atafika kwang'angayo anauzidwa kuti apeleke msembe yamwana wake oyamba ndipo mkuluyu apa anavomeleza kuti apeleka msembe mwanayo komatu mkuluyu anadzidzimuka asing'anga atamuuza kuti deal singatheke chifukwa mwanayo siwake ndipo magazi omwe akuyenda nthupi mwamwanayo ndi amunthu wina apa bamboyo mutu unawila chifukwa samatha kumvetsa zomwe ng'angayo imatathauza potengera kuti mwanayo wakula nayo ndipo mose wabadwa akumuona koma ng'angayo inakakamilabe kuti mwanayo siwake ndipo akuyenera kubweletsa mwana wake ndipo izi zinapangitsa kuti mkuluyu anganize zopita ku chipatala kukayesetsa pa chimatchini chija cha DNA test zomwe zinadzidzimutsa mkazi wake ndipo anadziwa kuti yalakwa ndipo amadabwa kuti kodi iyeyo wadziwa bwanji?ndipo zonse zinatheka mpaka zapezekadi kuti mwanayo siwake mkuluyo banja lathera pomwepo.

Langkzo:Palibe chobisika pansi pathambo ungabise bwanji tsiku limakwana ndithu lomwe Mulungu amaululitsa zonse zoniaika

06/01/2023

Nduna zina ntchito zitha pompano mukuona kuti amene angatsale ndindani?

06/01/2023

LILONGWE CITY COUNCIL YALAMULA KUTI ANTHU AYAMBENSO KUDYA DUDU.

Patangotha tsiku limodzi Lilongwe city council itatseka company ya Central Pottery ku Lilongwe kamba ka umve omwe umachitika pamalipa tsopano khosolo ya mzinda wa Lilongwe yapeleka chilolezo ku kampaniyi kuti ikhoza kupitili ntchito zake zogulitsa khuku za DuDu .

Malinanga ndi chithunzi chomwe chikuyenda mmasamba amchenzo apa Facebook komanso WhatsApp chikuonetsa nkhuku zili ku toilet ,nkhuku zimenezi ndizomwe anathu opanga Bussines ya nkhuku amangwilitsa ntchito pogulitsa anthu mmadera osiyana,siyana mdziko muno ena amagula nkhuku zopha kale enanso amagula nkhuku zamoyoyo koma malinga ndi anthu ena omwe talankhula nawo pamalopo anati chimbudzicho sikuti anthu amagwilitsa ntchito koma amangwilitsila ntchito kutaila magazi ankhuku koma anaonjezera kuti chongolakwika mchakuti nkhukuzo zimaikidwa pansi.

Address

Nyambadwe
Kabula
123

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when New Politics Magazine NPM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share