02/11/2025
BLANTYRE🇲🇼
*WOLEMBA MR PRESIDEÑT*
*RIP CHITIMBE*
*Kaswiri odziwika bwino poimba nyimba za chimalawi Collins Chitimbe watisiya usiku wathawa*.
Malingana ndi akubanja komanso ma report omwe Mpira Sports yapeza ndikulanda akuti a Collins Chitimbe yemwe ndi brother wawo wa Innocent Chitimbe yemwenso ndi kaswiri oimba komanso kulengezera mpira pa wailesi ija ya Mtiveni Radio akuti brother wawo wangodwala kwa masiku ochepa atapezeka ndi nthenda ija ya sugar.
Collins Chitimbe atisiya usiku wathawa kuchipatala chachikulu cha malamuro ku makwasa m'boma la Thyolo.
Mauthenga ochuluka akupelekedwa opeleka ulemu osiliza kwamalemuwa.Ife a mpira sports tikupepesa akubanja munyengo yowawitsayi.