
13/07/2025
Dzulo pa 12 July kunakoma ndi ku Capital City Motel mu nzinda wa Lilongwe pamene anakonza Phwando la Futali [Futali Party].
Monga mukuwona mu zithunzimo kunali First Grade Futali kwinaku akumwelera inu uku.
Shout Out to S Bizzo for a well decorated Futali Party.
Tikufuna chikondwelero ichi muchichitenso mu mizinda ya Mzuzu, Blantyre komanso Zomba.
Koma ?
?