Inno Wachiyao

Inno Wachiyao Arts and entertainment
(3)

hello Wachiyao ofetu takula tikufuna anyamata akutelo ma top fas anga number yake ili sefu
27/02/2026

hello Wachiyao ofetu takula tikufuna anyamata akutelo ma top fas anga number yake ili sefu

26/02/2026

akazi otaya mimbawa gayena yawo ili popano

25/02/2026

Kodi ndi comedy iti yomwe inakusangalasani kwambili ya ine ndipo mokunyadilani ndiponyako airtime kwa anthu 5 oyambilira kuyakha

24/02/2026

siyani ndikutengeka za pa dziko

Chabwino kuweruza si kwathu. Koma munthu woti Nyimbo zake zimalira Ku beer-hall akutaniko Ku birthday ya Prophet Shepher...
23/02/2026

Chabwino kuweruza si kwathu. Koma munthu woti Nyimbo zake zimalira Ku beer-hall akutaniko Ku birthday ya Prophet Shepherd Bushiri ? Inu, mpaka woyimba za kumidima kuyima pa gome loyeretsedwa? Si malodza awa? Inno Wachiyao

nkhani yovetsa chisoni yomwe yachitika ku Dowa zimayi wina wataya mwana atanamizidwa ndizibambo wina kuti amukwatila 😭 a...
23/02/2026

nkhani yovetsa chisoni yomwe yachitika ku Dowa zimayi wina wataya mwana atanamizidwa ndizibambo wina kuti amukwatila 😭 akampha mwanayu ndipo mwapulani yawo zatheka koma a police awamanga osewa

23/02/2026

TAUZIWENI UBWINO UMOZI WA TEBA MUKAUZIWA TIKUMANE MU COMMENT SECTION

alihamudulillah zanga elidza watuluka kundende patatha chaka
22/02/2026

alihamudulillah zanga elidza watuluka kundende patatha chaka

21/02/2026

nangati wazuka ndimoyo bale wanga yakhani moni uyu poonesa kuthokoza mulungu mwazuka bwanji

Ndani akukumbukira kulu uyu nakha amatani
19/02/2026

Ndani akukumbukira kulu uyu nakha amatani

Address

M1
Lilongwe Area 18

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Inno Wachiyao posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share