Nathenje Entertainment

Call Directions Contact the business

Nathenje Entertainment The Official page for Nathenje Entertainment and Nathenje Music Awards

  🤝🤝🤝
22/08/2026

🤝🤝🤝

🌈 Tili bhobho kamofi.
11/05/2026

🌈 Tili bhobho kamofi.

Zonena zambiri tilibe.. Ambuye odziwa kutothoza atothoze banja la a Mwasiya.. May her soul rest in peace 💔
28/04/2026

Zonena zambiri tilibe.. Ambuye odziwa kutothoza atothoze banja la a Mwasiya.. May her soul rest in peace 💔

Let's party.
28/03/2026

Let's party.

Mawa zipona uku
06/12/2025

Mawa zipona uku

  entertainment.@ #Woyimba Patience Namadingo ndi yemwe alandire mphoto zambiri ku mwambo wa chaka chino wa UMP Music Aw...
26/11/2025

entertainment.@ #

Woyimba Patience Namadingo ndi yemwe alandire mphoto zambiri ku mwambo wa chaka chino wa UMP Music Awards.

Namadingo alandira mphoto monga Artist of the year(Male), Song of the year Tuli, Best Humanitarian komanso Best Live Act.

Eli Njuchi komanso Tay Grin ndi omwe atsatira ndipo Eli alandira mphoto monga Album of the year Cifu komanso Best Afro-beats/Fusion Act.

Pomwe Tay Grin alandira mphoto monga Tourism Promotion Award komanso Global Impact Award.

Enanso omwe apambana ndi monga Jetu ngati Artist of the year (Female), Wyson Malakamu mnyamata wa Aumvere fungo ngati Best Innovative Sound, Joe Ikon ngati Best Amapiano Act, Masintha Women Choir ngati Best Gospel Act, Black Missionaries ngati Best Band.

Mwambo wopereka mphotozi uchitika mu mzinda wa Blantyre pa 20 mwezi wamawa.

(Wolemba born Chakhwantha)

25/11/2025

*Welcome to the Nathenje Music Awards!*

Ladies and gentlemen, artists, fans, and music lovers, get ready for an unforgettable night of rhythm, talent, and celebration as we kick off the upcoming *Nathenje Music Awards*!

This year’s ceremony promises to shine a spotlight on the best of Nathenje's vibrant music scene—from soaring Afro‑soul melodies to electrifying dancehall beats, innovative content creators to emerging stars lighting up the stage.

Inspired by the spirit of unity and creativity that runs through every corner of our Ghetto, the Nathenje Music Awards are a celebration of passion, hard work, and the power of music to bring us together.

From dazzling performances to heartfelt recognitions, we’ll honor the artists who’ve moved our hearts, the producers who’ve crafted unforgettable tracks, and the fans who keep the music alive.

Join us as we countdown to a night filled with amazing talent, surprise collaborations, and moments that will echo long after the music fades.

Let’s celebrate the sounds that define our culture and the voices that shape our future at the *Nathenje Music Awards*—where every note counts! 🎶✨

Get Set as we Launch Nathenje Music Awards 2025
23/11/2025

Get Set as we Launch Nathenje Music Awards 2025



Anthu okonda za Msangulutso okhala ku Nathenje boma la Lilongwe ayembekezere zabwino pamene gulu lina la achinyamata kudera-ku likhale likukhazikitsa ndondomeko yopereka mphotho kwa omwe akuchita bwino ku nkhani ya Msangulutsoyi yomwe izichitchedwa kuti Nathenje Music Awards.

Poyakhula ndi Nathenje Podcast, modzi mwa akonzi a phwandoli a Recal James ati cholinga cha chilinganizochi ndikufuna kuyamikira achinyamata omwe akuchita bwino ku nkhani za Msangulutso komaso kuwalimbikitsa omwe akuyamba kumene.

Iwo ati ndondomeko yopereka Mphothozi yomwe ichitike January chaka cha mawa ifikira madera a Nanjiri, Nayere, Nathenje, Matindi, Kamphata komaso Kalumbu.

"Pakali pano titha kunena kuti zokonzekera zonse kuti Nathenje Music Awards ikhazikitsidwe pa 30 November pano zili mkati, ndipo ife tikungopempha anthu osiyanasiyana omwe ali ndikuthekera kuti atipange Sponsor," anatero a James.

akatu kakhala koyamba kuti dera la Nathenje lipereke mphotho kwa achinyamata omwe akuchita bwino mu nkhani za Msangulutso.

Wolemba: Wiza Msanyama

Bail yomwe anapepha vj Ken  yavomerezedwa atapereka ndalama zokwana 100 thousand kwacha komaso kumakaonekera ku police k...
21/11/2025

Bail yomwe anapepha vj Ken yavomerezedwa atapereka ndalama zokwana 100 thousand kwacha komaso kumakaonekera ku police kamodzi pa week. Kupanga hand over ma pepala oyendera, kufikilaso pa 19 December pomwe bwalo lizaveso mlandu.

Side note.
Milandu ngat iyi athu achuma ndi odziwika bail sivuta. Panjaso phwedo UKu. Nde enanu kaya.

Address

Nathenje
Lilongwe

Telephone

+265990424332

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nathenje Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nathenje Entertainment:

Shortcuts

Share