Malawi Wathu

Malawi Wathu ✓News
✓Updates
✓Entertainment
✓Political events coverage
(2)

Bungwe la Football Association of Malawi lalengeza kuti nsika wogula ndi kugulitsa ma player wapakati pa Chaka watseguli...
25/08/2026

Bungwe la Football Association of Malawi lalengeza kuti nsika wogula ndi kugulitsa ma player wapakati pa Chaka watsegulidwa kuyambila lero mpakana pa 21 mwezi wa Seputembala

A Evalista Chisale amene ali akazi awo a wachiwiri kwa anduna owona za chitetezo cha mudziko Norman Chisale tsopano wasa...
25/08/2026

A Evalista Chisale amene ali akazi awo a wachiwiri kwa anduna owona za chitetezo cha mudziko Norman Chisale tsopano wasankhidwa kukhala wachiwiri kwa wa nkulu wa polisi. Deputy inspector General- administration. Congratulations

Apolisi ofufuza milandu yazandalama kumawa kuno amanga  yemwe anali wankulu oyang'ana za chitsankho a Andrew Mpesi
25/08/2026

Apolisi ofufuza milandu yazandalama kumawa kuno amanga yemwe anali wankulu oyang'ana za chitsankho a Andrew Mpesi

25/08/2026

Atsikana a modeling akuchilimikatu🤣🤣 Ntchito ilipo

MWANA WAPEPESA MUKHULULUKIRENIApology from S Khrizzy to Temwa Chawinga & Malawians He posts; KWA TEMWA CHAWINGA NDI MTUN...
25/08/2026

MWANA WAPEPESA MUKHULULUKIRENI

Apology from S Khrizzy to Temwa Chawinga & Malawians

He posts;

KWA TEMWA CHAWINGA NDI MTUNDU WA A MALAWI

Ine S Khrizzy pamodzi ndi team yanga tikupepesa kwa Temwa Chawinga ndi kwa a Malawi nonse kamba ka nyimbo yomwe tinatulutsa posachedwapa yotchedwa "Temwa Chawinga"
Potulutsa nyimbo yi sitimatanthauza kapena kufuna kusamupatsa ulemu Temwa Chawinga, koma tinazindikila mochedwa kuti nyimbo yi siinapeleke ulemu.
Pa chifukwa ichi, nyimbo yi taichotsa pa ma streaming platform onse ndipo tidakali opepesa kwa Temwa, ndi Mtundu wa a Malawi onse pa zomwe zachitika ndipo zinthu ngati izizi sizizachitikanso.

Sincerely,
S Khrizzy and Team.

25/08/2026

Ma model afikanso geji inatu🤣🤣Mmmm koma yah

24/08/2026

Head to Head challenge@ Miss World with our girl Ireen Navicha 🇲🇼

24/08/2026

Boma tipitiliza zitukuko zonse zinayamba ndi Chakwera komanso za tsopano -Chihana

24/08/2026

A Chakwera monga abusa akale kulimbikitsa a Malawi kuti mavoto asatigonjetse koma ife tiwagonjetse

24/08/2026

God fearing and free minded MG2 👏

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Wathu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category