Mwathu Graphics

Mwathu Graphics Creative graphic solutions for businesses, brands & individuals
(3)

Utha kumaona ngati akuikhoza koma Ayi ndithu ili bwinobwino....ndi switch imeneyo😂😂Kungosuntha screw driver PC yazimila ...
24/09/2026

Utha kumaona ngati akuikhoza koma Ayi ndithu ili bwinobwino....ndi switch imeneyo
😂😂Kungosuntha screw driver PC yazimila pompo

24/09/2026

Bodza la Designer
"Ndatsala pang'ono
Kumaliza"😂😂😂
Iwe munthu olo PC sudayatse

24/09/2026

😂😂😂😂😂😂😂even The Sound Engineer was shocked
🙌🙌

Sindidzaiwala tsiku limenelo kunada mwa masiku onse.......magetsi adazima ndipo after kudya chakudya chamadzulo, adatiit...
23/09/2026

Sindidzaiwala tsiku limenelo kunada mwa masiku onse.......magetsi adazima ndipo after kudya chakudya chamadzulo, adatiitana kuti tikapemphele tizikagona🥱

Ifetu basi kutambalala pamene paja titavala kabudula wathu ndekuti takhalira achikulirewa.

Pemphero Lili nkati magetsi adayaka ...aaahhhh magaye🙌🙌🙌🙌🙌

23/09/2026

Mkwiyo wa ngongole kulakalaka wina atangondiputa ndimukunthe😏🙄

I have an idea 💡 guys😂😂😂😂Kungochigoneka pansi ichi nkuika mattress pamwamba pake sibasi🫰🫰Odi nkavane ndi makolo..asadafu...
22/09/2026

I have an idea 💡 guys😂😂😂😂
Kungochigoneka pansi ichi nkuika mattress pamwamba pake sibasi🫰🫰
Odi nkavane ndi makolo..asadafumbwe Queen size yu

Auntie Agula Blender yanyuwani  nde ehhh asaone masuku tu
22/09/2026

Auntie Agula Blender yanyuwani nde ehhh asaone masuku tu

Pena zimangofunika kupempha mwachikulu...imafika nthawi kumabwela Auntie 😋😋
22/09/2026

Pena zimangofunika kupempha mwachikulu...imafika nthawi kumabwela Auntie 😋😋

ATI "Kodi ndalama zako umapanga nazo chani?????"😂😂😂😂Simungaivetse pashoni makosana
22/09/2026

ATI "Kodi ndalama zako umapanga nazo chani?????"
😂😂😂😂Simungaivetse pashoni makosana

Tikudikula Nsima tingomenya kaye ka quick snack  basi😌😌😌munadyako Polony?Kalibu polony!!!😋😋
22/09/2026

Tikudikula Nsima tingomenya kaye ka quick snack basi😌😌😌munadyako Polony?
Kalibu polony!!!😋😋

Address

Lilongwe

Telephone

+265997087210

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mwathu Graphics posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mwathu Graphics:

Shortcuts

Share