APM MY VOTE

APM MY VOTE Informing, Educating and Entertaining People

07/04/2026

Kod ndan amamutengela ku Ntoso akuluwa? Awawa nde kaya mulira mutobthola akulu

04/04/2026

Justice Dr Jane Ansah dzulo anali nawo pa Mwambo wa njira ya yantanda. God first

29/03/2026

Wachiwiri wakale kwa mtsogoleri wadziko Hon Khumbo Kachali wamasuliratu konko dzulo k*t palibe cholakwika k*tumiza Nduna ngat woimila a president

29/03/2026

Adadie kuswitilana ndi madam akunyumba kwao pamene amachokela mudziko la America

This too is love❤️

08/03/2026

Awawa akanapwetekana dzulo ku Chileka 🤣🤣

03/03/2026

Tinaonadi malodza mudziko muno Brian Banda sakunama🤣🤣

02/03/2026

Anyamata azikwanje a MCP akupitilizabe kuvulaza anthu ngakhale MCP inatuluka muboma

Mtsogoleri wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wanyamuka mudziko muno masanawa kupita ku dziko la South Africa...
01/03/2026

Mtsogoleri wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wanyamuka mudziko muno masanawa kupita ku dziko la South Africa komwe akagwile ntchito Zina

Mtsogoleriyu wanyamuka kudzela pa bwalo la ndege la Kamuzu International ku Lilongwe

01/03/2026

Mutharika alibwino kwambiri pankhani yopanga ziganizo kusiyana ndi Chakwera. Watelo modzi wa akuluakulu a MCP Alex Major

01/03/2026

I am the President of all regions. And People from all regions voted for me, so I'll try my best to share developments equally -APam

Address

Area 12
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when APM MY VOTE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to APM MY VOTE:

Share

Category