Tikoza Malawi

Tikoza Malawi MALAWIYU TIKOZA

09/02/2025

Akapanda kutsogolera business yehova oyendetsayo ayendetsa chabe mukhale onditetezera mulungu

09/01/2025

Nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yati kwabadwa Namondwe watsopano mu nyanja ya mchere ya India, kumpoto cha kumvuma kwa Madagascar.

Malinga ndi nthambiyi, Namondweyu amutcha kuti 'DIKELEDI'.

Nthambiyi yati pakadali pano, Namondweyu akusonyeza kuti afika m'nyanja ya mchere ya pakati pa maiko a Madagascar ndi Mozambique, akadutsa ku mpoto kwa Madagascar lamulungu pa 12 January.

Nthambiyi sinanene ngati Namondweyu akhudze nyengo ya dziko lino kapena ayi komabe yati ikutsatira mwachidwi kayendedwe ka Namondweyu ndipo ikhala ikudziwitsa mtundu wa a Malawi.

M'masiku angapo akudzawa mvula ikuyembekezeka kuchepa mphamvu m'madera a m'chigawo chakummwera ndi pakati chifukwa cha mphepo zosakhanzikika zochokera kumvuma.




Mverani KCR pa 107.6MHz kapena pa utatavu kudzera pa 👇🏾

https://live.netradio.pro/listen/kcr/radio.mp3

29/12/2024

With Daughter of Zion Phalyce Mang'anda – I just got recognized as one of their top fans! You are my mum

25/12/2024

Tsiku ndilimeneri chopempha changa mchakuti tisayiwalemo mulungu ndikufunirani khilisimisi yopambana zikomo

23/12/2024

Tiyeni timuyamike mulungu potidzutsaso ndimoyo lero

Akuti kunjoya avocado 🥑🥑🥑🥑🥑
28/09/2024

Akuti kunjoya avocado 🥑🥑🥑🥑🥑

Tsamba la zbs latsimikzira za ngoziy
27/08/2024

Tsamba la zbs latsimikzira za ngoziy


Apolisi atsimikiza kuti minibus yomwe yachitanso ngozi ndikupha anthu asanu mwini wake ndi yemwenso minibus yake idapsanso sabata latha.

Mneneri wa apolisi ku Kasungu, Joseph Kachikho wati mwini wa minibusyo ndi waku Mzimba.

Ngozi ya sabata latha anthu 26 anapsera mminibus momwemo pomwe ngozi ya lero anthu asanu ndiwo atsimikizika kuti amwalira pakalipano.

(by Noel Mkubwi-Kasungu:08/27/24)

Address

Lilongwe

Telephone

+265996091502

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tikoza Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share