Dalitso Chauluka

Dalitso Chauluka Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Dalitso Chauluka, Digital creator, Lilongwe.
(1)

08/09/2026

Zikuoneka ngati a ESCOM Azimitsa Dzuwa msimmene kulili

13/06/2026

Mwina mkutheka simudziwa tathauzo la malawi
Awa ndi amwu amene anachokela ku ku moto kkkk
" " yes in english flames of fire mwachidule dziko lathu limatathauza kuti tili pa motooo

18/01/2026
23/12/2025

kukweza misokho kenaka ndikutapak 1.9 billion malawi kwacha wa ku birthday party koma anatilodzayi anakativela chisoni sure

10/12/2025

Kusiyana Kwa DPP ndi MCP ndi ndi ma colours a mbendera basi

21/11/2025

Nayo DPP yabwela ndi yokweza misokho🤣🤣🤣 VAT kuonjezela,PAYE kuonjezela,ku airtel money kuponyakoso ka msokho kena maguy mutimalizatu??

#

28/09/2025

Big shout out to my newest top fans! Victor Lipenga, Ika Man, Patrick Pindani, Tockna Kadzuwa, Vîgo P Dailydreams, Tiquesam Gwantabosta, Rad Banda, Tay-coon Wachipala, Tiyanjane Nkhoma, Lameck Madembe

18/09/2025

kod azimayi amavala msalu za odya zake alibe mulandu aja sanali aku malawi?
chifukwatu Dr usi akungomenya ma 2 alipheee

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dalitso Chauluka posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Dalitso Chauluka:

Shortcuts

Share