DarlieMw

DarlieMw Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DarlieMw, Digital creator, Lilongwe.
(2)

02/07/2025

I accepted 4 fan badges from Cha Cha, Nasty C SA and 2 others.

02/07/2025

We have good ideas, but those with power and money control everything. The system doesn't let people with good ideas lead instead, it favors those with political power who steal billions. The constitution protects them, so they keep stealing and oppressing us. When we try to share our ideas, they shut us out. In Malawi, leaders use stolen money to bribe people. They support the youth by painting their bodies with paint, and they buy beer for the youth to dance in their political rallies. They call it youth empowerment, but it's just a trick Ukhuluku. God sees what's happening
.... ....

02/07/2025

Naye Tamia ja basitu wangoyingalula akuti zataniso kaya ndi boss lady wakidziko lakutali
Muti zakhalaso bwanji kod🤣🤣

13/06/2025

Big shout out to my newest top fans! Victor Lipenga, Ika Man, Patreek Pindani, Tockna Kadzuwa, Vîgo P Dailydreams, Rad Banda, Tay-coon Wachipala, Tiyanjane Nkhoma, Lameck Madembe

09/06/2025

zikayenda bwino tigawa ma data bundles pamudzi pano
Invite your friends to follow and like our page basitu

07/06/2025

Kodi mwanvaaa!!! Akuti report la ngozi yandege yomwe inapha wachiwili wakale kwa tsogoleli wadziko lino latuluka
Check the link in the comment section

03/06/2025

Wapolisi yemwe amagwira ntchito m'boma la Dedza a Eric Chasweka wadzipha podzimangilira m'nyumba yake.

Mneneri wa apolisi m'chigawo chapakati chakuzambwe, a Foster Benjamin watsimikiza za nkhaniyi kuti a Chasweka anafika ku ntchito komaliza lachisanu ndipo ataweruka sanabwelerenso m'masiku otsatira.

A Benjamin ati izi zinachitsa kuti apolisi anzawo apite kunyumba yake komwe anathyola chitseko chanyumbayi.

Iwo ati anapezaso kalata zauthenga otsanzika kwa mkulu wa polisi ya Dedza, makolo ake komanso bwenzi lake.

Source:Zodiak Online

01/06/2025


Kodi mwanva!!! Lero m'mawa, dziko la Russia linaphulitsa ndege ya Ukraine komanso milatho ina, zomwe zawononga kwambiri.

Ukraine, mobwezera, inatumiza ma drone ambirimbiri omwe anabisala mu mitengo awononga ndege za nkhondo za Russia zokwana 40, kuphatikizapo ma bomber, ndege zazikulu zankhondo, ngati Tu-95, Tu-22M3 ndi A-50 .komanso ma factory osungiramo ndege mkati mwa dziko la Russia.

Zotsatirazi zatsimikiziridwa ndi Ukraine ndi Russia. Panopa, Ukraine ikupitilizabe kuponya ma drone, ndipo mavidiyo akuwonetsedwa live pa ma TV akuluakulu padziko lonse.

Source: World Mainstream Media

President Putin wa Russia wakwiya kwambili

01/06/2025

Thawi yakwana tsopano kuti andale atipanikize ndi ma bonanza😂😂
Thawi yoseyi kaya analikuti

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DarlieMw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to DarlieMw:

Share