06/11/2021
Pasi pa Mntengo Lyrics
Artist: Clarence
Verse 1
Pasi pa Mntengo/
Ndipomwe pandionetsa mmene imasithira nyengo/
Ndinali pasi pompo suger akukwera Mntengo/
Zithu zokoma kudula amwene dziko lachinyengo/
Pasi pa Mntengo
Usiku pamakoma kukamba thano ndi agogo/
Malangizo ndi a daily kufuna tikule mwamwambo/
Manja Bible/
Tigawane malembo/
Uthenga ufale mpakana pothera phepo/
Ndi Pasi pa Mntengo
Pandidziwitsa wakutsina khutu ndi nasi/
Usasilire chuma cha enawa ncha magazi/
Ukafuna za bwino Yesu umulonde mapazi/
Ukazipeza Basii/
Pasi pa Mntengo
(Hook)
----------------------------
Verse 2
Pasi pa Mntengo
Pandidziwitsa m'bale papya tonola/
Sudziwa ntima wa Moto umatha kukuzimira/
Ukapeza mwai wa ntchito osausekelera/
Kuyang'ane chitsogolo sudziwa pothera/
Pasi pa Mntengo
Zonse ndikukamba ndadziwa pasi pa Mntengo/
Kukhala Hule, Mbava osewa sichisakha/
Koma akufuna ndalama amwene uphawi ndi chilango/
Kukhumba za mdziko/
Ana opanda mwambo/
Angogonana ndi azibambo/
Ndalama yatisocheletsa kusepha mseu nkulowa jungle/
Zithu sizikuyenda/
Angogawa matenda/
Sinanga ndalama yimatha kukana chishango/
(Hook)
---------------------------
Verse 3
Pasi pa Mntengo pandiuza
Dziko lili mu mdima/
Church ili mu ntima/
Nthawi simayima/
Mphavu zili mu ndalama/
Mu Boma muli kunama/
Chilungamo chili mwa Ana/
Uphawi muli kuphana/
Mchikondi kukhumudwitsana/
Nzeru nkugawana/
Uchimo nkujahena/
Kukapya ndi Moto ndikufuna/
Kukhala chiDakwa si umuna/
Ndalama ndi Satana/
Pasi pa Mntengo panatero i believe sipa nama/
(Hook)
----------------------------
The end😁