Collings Massinah

Collings Massinah Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Collings Massinah, Lilongwe.
(9)

04/10/2025

Every successful person has a painful story.
Every painful story has a successful ending.
Accept the pain and get ready for success. 😋😋

25/09/2025

PATUMA KUSANVA

Ali ndi dzana 6 mama changu ndichedwatu kusukulu ok mwana wanga koma kodi umafuna uzakhale ndani ukazamaliza sukulu,,,,

ndimafuna ndizakhale dokotala ok mwana wanga patuma anali ndi mayi abwino omwe amamulangiza tsiku ndi siku kuchokera ali mwana zokhuza makhalidwe abwino ,,,,

Atafika std 8 anapeza kachibwez koma poti onse anali masupuni.patuma samaona phindu poti adawa adali amaluzi apatuma anayamba kusukika nde ankafuna tindalama aziphodera.😂

patuma anathesa ndikuyamba chibwez ndi aphuzisi ake moti mpaka anagonana kangapo konse

nkhani inavuta nkazi wamphuzisiyi atayinva anakwiya zed ndipo anapita kusukulu konko namugwila patuma

anamumenya mpaka thapsa anamuvula zovala zonse ndi pant yemwe.kuti aone chomwe akusatira.amunake.

Pangan follow👉 Collings Massinah kuti musaphonyedwe

25/09/2025

Analibe ntengo ogwira tsikanayo ndiye anakatani iye adapakulisa kuti apeze chokudya ndipogona..

kalionela avulalitsa zione sikanayu anali okongola zed ndipo amachoka pankomo pakwawo osadya pena ndiye chimakhala chithu chomwe amawauza amzake pafupi pa fupi..

njala ikundiwawa poti sindinadye bambo anga anapuma ntchito ndipo akudila ndalama za peshoni ndiye kupeza ndalama kukumakhala kowavuta..

aaaaaaaaa iwe tsikana wabwino bwino ngati iwe chochita chikukusowa aaaaa koma aa gerl muli serious? tangoona ma phone omwe tikuyuza simanyakatu inu munakaphabe sikizi tobwa tobwa inu a girl mulibe look sharp

Anatelo wangi pomukopa zioneyo ndipo zione adafusa look sharp nde chani a girl ndithandizeni ine nzanu....

mmmmm inu a girl ndikamodzi kokhatu mfwenfwe kuno ndipo a girl simungakhale manyaka

zione ntima pha pha pha akaganizira uphawi.omwe uli kwawo ndipo linali loweruka anamutenga zione kukayenda nawe...

Ndipo ali kuyenda wangi phone inaitana pakuyankha kwake anvekele mmm inu mpaka puleni ndi oyamba kumenetu ,,,, aaaa iwe mesa ndi ndalama kodi? wangi anavomeleza kuti chabwino bho bho...

kusogolo kwawo kunali galimoto ndipo inayima anamuuza zione takwera zione anali odabwa ndipo anafusa nakha inuyo mmmm a girl look sharp tu paja ife timapelekeza iwe

Ikupitililabe....

Follow 👉 Collings Massinah

21/09/2025

JOYCE 💔 PART 5

Ukapanga chipongwe munthu supanga zolongosoka ndipo patadusa ma tsiku ochepa bambo a Joyce anapenga misala ndipo amazilumaluma okha okha ndipo anthu sanadabweso poti anaziwa kuti masoka akuwasata zimu wankaz wake ukumuzuza

Ndipo ngakhale Joyce amapita kwama prophet osiyanasiyana koma be sanakwanise kukachilabe mpaka mimba ija inakwana miyezi 19 apo anthu anayamba kukambilana kuti mmmm mwana yo ngat ndiwamamuna azabadwa ndi ndevu kale

Atayima mutu joyce mayi ake atafa chifukwa chaiye ndi bambo ake ndipo bambo ake atapenga misala koma so iyeyo mimba yomwe anagona ndi bambo akeyo mpaka miyezi 19

Apa anaganiza zongokapanga za opaleshoni kuti apeze ntendere poti anali kusausika ndi ululu tsiku ndi tsiku

Ndipo ma siku akuchipata kuti akapangidwe opaleshoni atafika ndipo iye sanamulore kuti afe koma so kuti mwana wake afe koma anve kuwawa

Joyce anapangidwa opaleshoni koma pomwe ankamutulusa mwana a anali be mwendo umodzi ndipo mwana yo anali wankaz anali wakhulu choncho poti anabadwa mwezi wa 20

JOYCE anatulusidwa kuchipatala ndipo atafika kwawo anabisa mwana wake kuti anthu Asamuone poti alibe mwendo umodzi ndipo apo anayamba kuboweka nawe mwana yo ndipo anayamba kuganiza kuti ndivuto loonjezera poti anthu azimuseka ndikumutoza

Joyce mabala ONSE ankangophulika ndipo kumangonyeka moti madokotala anamuuza kuti sangakwaniseso kusoka ndipo mwana uja anali ovuta akayamba kulira zinali ngat akukumba mabala ndipo amaboweka nawe kambiri

Patadusa ma week awiri Joyce atatopa ndiululu koma so kutozedwa anaganiza zongozipha kuti akapume koma mmm vula ikakuona lisiro sikata Joyce anatenga chingwe ndipo atazinyonga anthu anamupulumusa kotero anamupitisa kupolisi ndipo apolisi atamuona Joyce nyengo yomwe Ali anangomutulusa

Ndipo apo Joyce alibe ntendere ndipo alibe mwayi or pang'ono

Osama panga chipongwe anthu omwe amatikonda koma so omwe timawakonda osamayiwala makolo Ali ngat Mulungu wanthu wachiwiri

Ikupitililabe.........

MA PART AMBUYO UKU 👉Collings Massinah pangan follow page kuti musaphonyedwe

19/09/2025

JOYCE 💔💔 PART 4

Aulowa umasiye Joyce kamba ka usilu wake mayi ake amwalira kamba kazilakolako zake apa bambo ake ndi anthu Ena anapanga madongosolo amaliro

Kenako bambo a Joyce apeza mwayi omasuka sinakha apa sangamazembereso koma azingogonana ndi mwana wawoyi momamasuka

Apa patapita matsiku ochepa chichitikileni maliro mudzimo mudabwera prophet ndipo anthu amakhamukira kumeneko kuti akathandizidwe poti amapanga zodabwisa prophet yi

Ndipo Joyce anali mugulu lokafuna thandizo poti mimba yakeyi inakwana miyezi 13 asanachirebe ndipo anthu anayamba kunena zambiri poti mbiri sigonera anachitawo ndi malaulo ndi mwikho mmm mwana opanda matha

Anthu Ena azikhulupiliro anayamba kumuuza kuti zimu wa mayi ake ndi omwe akumupangisa zimenezo zimu wawo udakali okwiya ndipo muzisamba anauzidwa kuti sakhalisa amwalira

Apa Ali kalikiliki kupephela kuti Achille

To be continued.....

MA PART AMBUYO ONSE ALI UKU 👉Collings Massinah GINDAN MUPANGEKOSO FOLLOW KUTI MUSAPHONYEDWE

You can also follow on Instagram to see more.
19/09/2025

You can also follow on Instagram to see more.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Collings Massinah posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share