TREND WATCH

TREND WATCH PROFESSIONALISM IS WHAT MATTERS

Wisdom S Yotamu was born in a family of six children.His Father is Semeon Yotamu and mother is Agness Chiwoko .He has his elder brother by the name Haswel.Wisdom has got his twine brother called Wiseman they were born on 02 October 2000.He has also three younger sisters by the name Beauty,Takondwa and Lucy inorder.Wisdom is poet and he has been doing this since his childhood.

27/07/2025

Dr Dalitso kabambe achpani cha UTM asankha Mathews Mtumbuka achipanichi kuti ndiwo akhala running mate wawo Ku zisankho zapa 16 September 2025.

Ku BICC mu mzinda WA Lilongwe kwadzadza Ndimakaka achipani cha UTM pomwe Dalitso kabambe akukapereka zikalata zake zomul...
27/07/2025

Ku BICC mu mzinda WA Lilongwe kwadzadza Ndimakaka achipani cha UTM pomwe Dalitso kabambe akukapereka zikalata zake zomulora kupikisana nawo ngati president wadziko lino.

Akabambe afika akuyendetsa giledala pambuyo pawo pali a Newton Kambala akuyendetseso yawo zomwe zikupenekera kuti mwina atha kukhala running mate wawo.

Wolemba (WisdomWisdom S Yotamu 27/07/2025)

Pamene nthawi ikupitabe chitsogolo kuti tifike 9 koloko A Malawi ambiri mitima yawo ili dyoko dyoko kuti awone  running ...
25/07/2025

Pamene nthawi ikupitabe chitsogolo kuti tifike 9 koloko A Malawi ambiri mitima yawo ili dyoko dyoko kuti awone running mate yemwe ayende limodzi Ndi Professor Author Peter Muthalika a chipani cha DPP.

Manong'onong'o akhala akuveka kuti chipanichi chitha kuchita mgwirizano Ndi chipani cha UTM koma kukambirana kwawo kwafera mmazira pomwe akanika kuvana za yemwe atsogolere mgwirizanowo.

Dzulo chipanichi chapanga mgwirizanowo oyendera limodzi Ndi chipani cha AFORD.

Wolemba Wisdom S Yotamu
(25/07/2025

CHENJEZOKwa nose amene mukuchoka Mzuzu kupita Karonga kapena  kuchoka karonga kupita Mzuzu dziwani kuti mkatikati mwa ms...
12/07/2025

CHENJEZO

Kwa nose amene mukuchoka Mzuzu kupita Karonga kapena kuchoka karonga kupita Mzuzu dziwani kuti mkatikati mwa mseu wachiweta pa Namiyashi pali truck yomwe yatseka nseu.

Chonde ma driver yendan mosamala tetezani miyoyo

WHAT HAS REMAINED IS ECONOMICALLY INDEPENDENCE AS A Nation 🇲🇼🇲🇼
06/07/2025

WHAT HAS REMAINED IS ECONOMICALLY INDEPENDENCE AS A Nation 🇲🇼🇲🇼

TREND WATCH The Malawi national examination board (MANEB) says all is set to administer the 2025  Malawi  School Certifi...
30/06/2025

TREND WATCH

The Malawi national examination board (MANEB) says all is set to administer the 2025 Malawi School Certificate of Education (MSCE) Examinations.

A total of 202,940 students are expected to sit for the 2025 MSCE examinations starting tomorrow 1 July.

According to MANEB, out of the 202, 940 students, 97, 489 are female candidates while 105,451 are male candidates.

MANEB has also assured the general public that it has put in place strict measure to ensure that there is tight security in all examination centres in the country.

The exams are expected to commence with agriculture paper 1 starting from 8 o'clock in the morning.

By Denis Malota, Blantyre (30/06/2025)

TREND WATCH

Team ya Silver strickers yalengeza za kuchoka kwa osewera wake pa wa pakati Chimwemwe Idana.Polemba pa tsamba la mchezo ...
30/06/2025

Team ya Silver strickers yalengeza za kuchoka kwa osewera wake pa wa pakati Chimwemwe Idana.

Polemba pa tsamba la mchezo la Facebook timuyi yayamikira osewerayu kaamba ka kudzipereka kwake munthawi yomwe wakhala akutumikira timuyi.

Osewerayu adalowa timu ya Silver strickers mchaka cha 2023 ndipo wathandizira masewero osiyanasiyana omwe timuyi yakhala ikusewera ndipo adali katswiri ofunikira yemweso adathandizira kuti timuyi ipambane chikho cha TNM Super league chaka chatha.

Sizidadziwikebe kuti chitsogolo cha osewerayu chikhala chotani koma kafufuku yemwe TREND WATCH yachita wapeza kuti osewerayu atha kulowera m'dziko la Zambia komwe akakhale akutumikira timu ya ZANAKO F.C.

Finally Wespar  drops his new music video akuti Pastor.uyuyu eeeeh tinganene kuti sazatheka coz zomwe wapanga umumu nde ...
23/06/2025

Finally Wespar drops his new music video akuti Pastor.

uyuyu eeeeh tinganene kuti sazatheka coz zomwe wapanga umumu nde ndizachabe.

Put some respect on this guy mukhoza kumahater oyimba enawo koma uyuyu nde panopa ali mu level yake yake ndithu.

Olo tangowonerani zimene waipanga video imeneyi akulu akulu kuyamikira pa zithu zabwino ngati izi ndikofunika kwambiritu.

Watch and enjoy new video from Wespar x Kids cana here👇

Vitumbiko Mumba Resigns from MCP NEC, Cites “Primitive Politics” and Lack of Internal DemocracyBy Wisdom Yotamu (17/06/2...
17/06/2025

Vitumbiko Mumba Resigns from MCP NEC, Cites “Primitive Politics” and Lack of Internal Democracy

By Wisdom Yotamu (17/06/2025)

Vitumbiko Mumba has officially resigned from the Malawi Congress Party (MCP)’s National Executive Committee (NEC), citing deep frustrations with what he describes as undemocratic practices and internal power struggles.

However, Mumba has made it clear that he remains a committed member of the party and will continue to support President Lazarus Chakwera.

In a public statement released via his social media platforms, Mumba revealed that his decision came after months of reflection. He said he wants to focus on meaningful development issues in his constituency rather than what he called “man-made small-mega battles” within the party.

“It will help me focus on issues that matter than man-made small-mega battles aimed at ‘kuthana’. It is just a waste of time and I no longer have time for such,” he said.

Mtsogoleri wakale wadziko la Zambia Edgar Lungu wamwalira mdziko la South Africa.Malingana ndinyumba yofalitsa mawu ya m...
05/06/2025

Mtsogoleri wakale wadziko la Zambia Edgar Lungu wamwalira mdziko la South Africa.

Malingana ndinyumba yofalitsa mawu ya mdzikolo ya Diamond TV alungu kumawaku anali ku a kupweteka pa mtima
Aku banja asadalankhuleko pankhaniyi

Address

Lilongwe

Telephone

+265990166355

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when TREND WATCH posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to TREND WATCH:

Share

Category