
26/07/2025
Mtsogoleri woyendetsa masewero a mpira wamanja m'dziko muno Vitumbiko Gubuduza kumasanaku anali nawo ku Area 30 komwe kuli mpikisano wachigawo chapakati mu mpikisano wa One Nico Top 12.
Umu ndi momwe zayendela mu ndime ya magulu;
1. Blue Eagles 36:16 Boma Stars
2. MDF Lioness 29:27 Dyna
3. Blue Eagles 55:18 KIA
4. MDF Lioness 43:19 Atlas
5. Dyna 39:10 Atlas
6. Vanessa Sisters 31:33 Civonets
7. Young Eagles 62:14 Armour Batalion
8. Civonets 13:61 MDF Lioness Youth
9. Vanessa 66:11 MDF Lioness Youth
Zateremu ma timu awiri mu gulu lililonse adzigulira malo mu ndime yamatimu asanu ndi atatu (8), ndipo ma timu akhale akukumana motere:
1. Blue Eagles vs Armour Batalion
2. Boma vs Young Eagle
3. Civonets vs Dyna
4. MDF Lioness vs Vannessa
Ma-timuwa akhala akukumana mawa.
Wolemba: Wilfred Golden