News 265

News 265 Your trusted source of news from Malawi and beyond.
(1)

 Mamembala a MFF awachenjeza kuti asayankhulepo pa nkhani yokhudza mtsogoleri wa dziko lino ndi wachiwili wakeA Bonface ...
02/08/2026



Mamembala a MFF awachenjeza kuti asayankhulepo pa nkhani yokhudza mtsogoleri wa dziko lino ndi wachiwili wake

A Bonface Joseph ndi a Kinka Makoloni omwe ndi atsogoleri a bungwe la Malawi Freedom Fighters (MFF) achenjeza mamembala a bungwe lawo kuti asayankhulepo pa ubale wa Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa Dziko lino a Dr. Jane Ansah, ndi Mtsogoleri wa dziko lino, a Arthur Peter Mutharika (APM) ngati alibe umboni.

Mu chikalata cha atolankhani chomwe News 265 inapeza la mulungu a Joseph anachenjeza mamembala a MFF kuti asagwiritse ntchito dzina la bungweli polankhula pa nkhaniyi.

“MFF imakhulupirira kwambiri ufulu woyankhula, koma bungwe lathu silinafikebe pa udindo wovomerezeka pa nkhani imeneyi,” a Joseph anatero. “Chifukwa chake timalangiza mamembala athu ndi omenyera ufulu athu kuti asayankhule pa nkhaniyi pogwiritsa ntchito dzina la MFF.”

Atsogoleri onse awiriwa ananenetsanso kufunikira kokhala ndi umboni musanalankhule poyera:
"Joseph ndi Pulofesa Kinka alimbikitsa omenyera ufulu kuti asayankhule pa ubale wa a Jane Ansah ndi APM ngati alibe umboni ndi chidziwitso cholondola.”

Joseph adanenetsanso omwe ali ndi udindo wolankhula m’dzina la MFF:
"Ndi Mtsogoleri wamkulu, Prof. Kinka Makoloni, ndi Mlembi wamkulu, Bonface Joseph, okha ndi omwe ali ndi udindo wolankhula m’dzina la bungwe.”

Chenjezoli likubwera pambuyo poti Sylvester Namiwa, Mtsogoleri wamkulu wa CDEDI, posachedwapa ananena kuti Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa Dziko, a Jane Ansah, adzakhala Mtsogoleri wa Malawi m’miyezi iwiri ikubwerayi. Namiwa adafunsanso mafunso okhudza "motani, chifukwa chiyani, ndipo APM adzakhala bwanji.”

Poyankhapo pa kumangidwa kwa Namiwa, Joseph anayamikira a malamulo ndipo anapempha mabwalo a milandu kuti achite chilungamo:
"Bonface Joseph ali ndi nkhawa monganso wina aliyense waku Malawi.”
"Tikuyamika a malamulo chifukwa chomanga Namiwa wa CDEDI. Tsopano tikupempha a mabwalo a milandu kuti achite milandu mwachilungamo kuti chilungamo chipambane.”

Anadzudzulanso atsogoleri andale chifukwa chothandiza omwe amangidwa:
“Zikudetsa nkhawa kuona atsogoleri a zipani zandale omwe akufuna kulamulira dziko mwa demokalase akupereka chithandizo ndi mphamvu kwa anthu omwe amangidwa chifukwa cholankhula zotere.”

MFF inatseka ndi pempho kwa dziko lonse:
"Tikupempha a Malawi onse kuti apitirize kupemphera pa dziko lathu ndi atsogoleri ake kuti Malawi akwaniritse zolinga zake zosintha ndi chitukuko. Mulungu adalitse Malawi.”

Apolisi sanatsimikizirebe milandu yeniyeni yomwe Namiwa akukumana nayo. Bungwe la CDEDI silinaperekebe yankho lovomerezeka mpaka pano.

Bambo Agostino Vida, azaka 30, omwe mutu wawo sugwira apha a John Shuga azaka 60, ku Mulanje kwa TA Mabuka mudzi wa Moth...
02/08/2026

Bambo Agostino Vida, azaka 30, omwe mutu wawo sugwira apha a John Shuga azaka 60, ku Mulanje kwa TA Mabuka mudzi wa Mothiwa.

Agostino omwe amakhala kumphanga lina mu Phiri la Mulanje, anasemphana chichewa ndi a Shuga pankhani ya makaka omwe Gostino anaba.

A Vida anachita kuwaduladula a Shuga ma piece ma piece powaphapo.

Thupi la katswiri wodziwika bwino pankhani zoulutsa mawu, Mbumba Nkhoma lalowa m'manda lero ku Area 18 mu mzinda wa Lilo...
02/08/2026

Thupi la katswiri wodziwika bwino pankhani zoulutsa mawu, Mbumba Nkhoma lalowa m'manda lero ku Area 18 mu mzinda wa Lilongwe.

Mbumba adamwalira pa ngozi yomwe idachitika ku Ntcheu lachisanu lapitali.

  A Bayana Chunga omwe ndi m'modzi mwa akuluakulu ku kampani yofalitsa nkhani ya Times Group ati malemu Mbumba Tiyamike ...
02/08/2026



A Bayana Chunga omwe ndi m'modzi mwa akuluakulu ku kampani yofalitsa nkhani ya Times Group ati malemu Mbumba Tiyamike Nkhoma anali munthu odalirika pa kagwiridwe kantchito ku kampani ya Times.

A Chunga ati Mbumba wathandiza kwambiri kupititsa patsogolo ntchito zosiyanasiyana kukampaniyi.

Izi amayankhula pamwambo wa maliro omwe ukuchitikira pa Chikuluti CCAP ku Area 49 mumzinda wa Lilongwe.

Mbumba anatisiya pa 31 July chaka chino m'boma la Ntcheu pangozi ya galimoto pomwe ankapita ku Lilongwe.

Walemba: Yohane Shepherd Maliro

Mphatso Phiri anali nawo pa ngozi yomwe yachitika ku ntcheu dzulo ndipo maliro ngoyika lero kwa mchotseni mudzi mwa shug...
02/08/2026

Mphatso Phiri anali nawo pa ngozi yomwe yachitika ku ntcheu dzulo ndipo maliro ngoyika lero kwa mchotseni mudzi mwa shuga ku Mwanza.

  Police Officer Collapses, Dies on Duty in Lusaka The Zambia Police Service regrets to confirm the sudden death of Cons...
02/08/2026



Police Officer Collapses, Dies on Duty in Lusaka

The Zambia Police Service regrets to confirm the sudden death of Constable Mumbuna Namakando of Kabwata Police Station. He collapsed while on duty near Lewanika Mall along Mosi-O-Tunya Road on July 31, 2026, around 22:00 hours, in circumstances yet to be established.

He was rushed to Chilenje Level I Hospital, where he was pronounced dead on arrival.

His body has been taken to the University Teaching Hospital (UTH) Mortuary pending a post-mortem examination to determine the cause of death.

The Zambia Police Service extends its heartfelt condolences to the family, friends, and colleagues of the late Constable Namakando.

Further information will be communicated as investigations progress.

Issued by:
Godfrey Chilabi
Public Relations Officer

𝗠𝗜𝗦𝗔 𝗠𝗔𝗟𝗔𝗪𝗜 𝗠𝗢𝗨𝗥𝗡𝗦 𝗧𝗜𝗠𝗘𝗦 𝗚𝗥𝗢𝗨𝗣 𝗣𝗥𝗘𝗦𝗘𝗡𝗧𝗘𝗥, 𝗣𝗥𝗢𝗗𝗨𝗖𝗘𝗥 𝗠𝗕𝗨𝗠𝗕𝗔 𝗡𝗞𝗛𝗢𝗠𝗔MISA Malawi is deeply saddened by the untimely death of ...
02/08/2026

𝗠𝗜𝗦𝗔 𝗠𝗔𝗟𝗔𝗪𝗜 𝗠𝗢𝗨𝗥𝗡𝗦 𝗧𝗜𝗠𝗘𝗦 𝗚𝗥𝗢𝗨𝗣 𝗣𝗥𝗘𝗦𝗘𝗡𝗧𝗘𝗥, 𝗣𝗥𝗢𝗗𝗨𝗖𝗘𝗥 𝗠𝗕𝗨𝗠𝗕𝗔 𝗡𝗞𝗛𝗢𝗠𝗔

MISA Malawi is deeply saddened by the untimely death of Times Group Presenter and Producer Mbumba Nkhoma.

Mbumba died at the age of 31 in a road accident on Friday, July 31, 2026.

She joined Times Group in February 2026. Before that, Mbumba worked for Groove 100 FM and Story Club FM.

Mbumba was one of the up-and-coming media personalities who fully embraced digital platforms as platforms for freedom of expression and storytelling. She will be remembered for using the media and her talent in promoting arts, culture and free speech. The Malawi media will dearly miss her charming personality.

Burial is taking place at Area 18 cemetery in Lilongwe today Sunday, August 2, 2026.

Our condolences go to the Nkhoma family, colleagues at Times Group, Groove 100 FM and Story Club FM and the entire media fraternity.

May Mbumba's soul rest in eternal peace.

Signed
Felix Washon
𝗖𝗵𝗮𝗶𝗿𝗽𝗲𝗿𝘀𝗼𝗻, 𝗠𝗜𝗦𝗔 𝗠𝗮𝗹𝗮𝘄𝗶

  60-YEAR-OLD MAN ALLEGEDLY KILLED AND DISMEMBERED IN MULANJE OVER STOLEN CASSAVAA shocking and tragic incident has been...
02/08/2026



60-YEAR-OLD MAN ALLEGEDLY KILLED AND DISMEMBERED IN MULANJE OVER STOLEN CASSAVA

A shocking and tragic incident has been reported in Chipoka Village, under Traditional Authority Mabuka, on the slopes of Mount Mulanje.

A 60-year-old man, John Shuga, was allegedly killed and dismembered by Agostino Vida, 30, of Mothiwa Village, TA Mabuka. According to reports, the suspect, who is said to have been living in a cave on Mount Mulanje, allegedly cut the victim's body into more than ten pieces before scattering the remains.

The deceased, Mr. Shuga, lived in Chipoka Village and worked for STECO, a tobacco-growing company. He also cultivated cassava on the slopes of Mount Mulanje, where he processed it into dried cassava chips ("makaka"). The suspect is reported to have lived for an extended period in a cave located between two large rocks on the mountain.

On 30 July 2026, Mr. Shuga reportedly discovered that some of his dried cassava had been stolen. He allegedly suspected Mr. Vida of the theft and is said to have gone into the mountain to confront him.

It is believed that the two met at the cave, where an altercation broke out. Investigators allege that Mr. Shuga was overpowered and killed before his body was brutally dismembered.

When police and medical personnel, assisted by members of the local community, arrived at the scene, they recovered human remains from different locations around the area. The remains were later identified by relatives as those of Mr. Shuga. Police also reportedly found bloodstains leading from inside the cave to the area where parts of the body had been discarded.

The suspect is currently in police custody in Mulanje.

Zochitika pa Mpanje

  Bambo Zonyera Zambuzi, omwe anthu owanyadila amawati Azonyera, ndi omwe asankhidwa kuti akhale Mfumu (Traditional Auth...
02/08/2026



Bambo Zonyera Zambuzi, omwe anthu owanyadila amawati Azonyera, ndi omwe asankhidwa kuti akhale Mfumu (Traditional Authority) kachindamoto, kutsatira kumwalira kwa a Kachindamoto omwe anamwalira pa 13 August 2025.

Azonyera ndi omwe anali oyenela kulowa pa mpando wu ndithu, koma mfumu yayikulu ya Angoni, Inkosi ya Makhosi Gomani V, idakana kuwavomeleza chifukwa mkuluyi anali asanalongosole madongosolo ena.

Azonyera anali okwatira ndipo ali ndi ana omwe azalowe ngati mfumu iwowa akazamwalira. Chinangovuta kuti sanapeleke malowolo. Akuti munthu akapanda kupeleka malowolo amakhala kuti mwambo wa chingoni sanakwanitse onse, ndipake a Zonyera anawakaniza.

Apopo malowola apanga dongosolo ndipo Mfumu yayikulu Gomani V yavomela kuti akhalano TA Kachindamoto.

  Police launch manhunt for businessman's murderers near Dudu Poultry FarmLilongwe Police has launched investigations fo...
02/08/2026



Police launch manhunt for businessman's murderers near Dudu Poultry Farm

Lilongwe Police has launched investigations following an armed robbery incident that left a businessman dead and a security guard seriously injured near Dudu Poultry Farm along the Malangalanga ADMARC Forest on July 30, 2026.

The deceased has been identified as Emmanuel Mangani, 32, a businessman based at Mitundu Trading Centre while the injured victim is Chikumbutso Mayola, 35, who works as a security guard at Malangalanga ADMARC.

Preliminary investigations indicate that Mangani (deceased) was travelling in his two-tonne pickup truck, registration number NS 8094, from Mitundu to Dudu Poultry Farm to purchase approximately 250 chickens valued at about K4.25 million.

Upon reaching the Malangalanga Forest near the poultry farm at around 23:00 hours, he was allegedly confronted by two armed criminals who shot him in the head, killing him instantly, before robbing him of the cash.

Security guards from Dudu Poultry Farm responded after noticing the robbery in progress, forcing the suspects to flee towards the nearby Malangalanga ADMARC Forest.

As they escaped, the suspects allegedly opened fire at security guards in the area.

During the exchange, Mayola sustained a gunshot wound to the lower jaw and was rushed to Kamuzu Central Hospital, where he is still receiving treatment.

Police found Mangani's body lying outside the passenger's door of his vehicle, which had come to rest on the roadside embankment.

Law enforcers recovered a cartridge from the vehicle's dashboard, while the driver's door window had been shattered.

Preliminary observations suggest that the deceased and the assailants were inside the vehicle during the attack.

The body of the deceased was taken to Kamuzu Central Hospital mortuary for a post-mortem examination.

Police have launched a manhunt for the suspects, who remain at large.

Emmanuel Mangani hailed from Nchetechete Village, Traditional Authority (T/A) Kalumo,Ntchisi, while Chikumbitso Mayola comes from Ntondo Village, T/A Khombedza in Salima District.

CREDIT:
Inspector Hastings Chigalu
Lilongwe Police PRO

Address

Lilongwe

Telephone

+265992068401

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when News 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to News 265:

Shortcuts

Share