Malawi voice

Malawi voice The most influential, trusted and loved source of verified news outlet. It is fast and up to date. your most trusted outlet.
(1)

ZILI KU DPP UKU NKHONDO YA NGITAWO!Minister of Foreign Affairs George Chaponda has been moved from seat number 2 to seat...
14/07/2026

ZILI KU DPP UKU NKHONDO YA NGITAWO!
Minister of Foreign Affairs George Chaponda has been moved from seat number 2 to seat number 9.

On the other hand, Hon. Roza Mbilizi Fachi has been promoted from seat number 9 to seat number 2.

Zangoyamba kuli zambiri muzimva. Chaponda ulendo uwu kaya sanabenso chimanga kaya

Clean money hurts, no money is earned clean ma guy
13/07/2026

Clean money hurts, no money is earned clean ma guy

Nduna yoona za masewero Alfred Gangata yadabwitsa aphungu pomwe mayankho ake ku mafunso omwe anafunsidwa amangoti "Noted...
13/07/2026

Nduna yoona za masewero Alfred Gangata yadabwitsa aphungu pomwe mayankho ake ku mafunso omwe anafunsidwa amangoti "Noted."

Phungu wa dera la Lilongwe City Kamphuno a Khadija Leah Chunga anapempha ndunayi kuti ithandize kupezera anyamata a dera lake ngongole pofuna kuwapatsa chochita, iwo anangoyankha kuti "Noted."

Chunga anapeleka chitsanzo cha zomwe zachitika lero kwa Chinsapo komwe kunali kulimbilana mgodi kuti izi zasonyeza kusowa chochita kwa anyamatawa.

Aphungu onse omwe anafunsa ndunayi monga zokhudza ma technical college, kuyima kwa Stadium ya Mbelwa angoyankhidwa kuti "Noted."

13/07/2026

Akuti.mukuwaphelanji azimai, DPP anthu akukudandaula seriously. Within your party anthu akulira, outside nde its worse

Sikulibwino Ku Chinsapo 2 Pamsika; Ma Business Asokonekera.___Pali ziwawa zomwe zayamba kutsefukira mumsikawu, pomwe ant...
13/07/2026

Sikulibwino Ku Chinsapo 2 Pamsika; Ma Business Asokonekera.

___Pali ziwawa zomwe zayamba kutsefukira mumsikawu, pomwe anthu akumenyana. Ena atenga zida zakuthwa ndi mipeni, ndipo achinyamata akukanganirana migodi m'derali.

Akutitu ma MP a DPP akubweletsa bill yomwe itasinthe malamulo a dziko lino. 1. Akuti president adzikhala pa mpando kwa z...
13/07/2026

Akutitu ma MP a DPP akubweletsa bill yomwe itasinthe malamulo a dziko lino.
1. Akuti president adzikhala pa mpando kwa zaka 7 osatinso 5 ayi cholinga wina asazamalize term yake oho
2. Akuti nawonso ma MP adzikhala pa mpando wawo kwa 7 years ndithu. Koma ma counsellor palibe chitasinthe.
3. Akuti ma MP adzilandila ndalama mu moyo wawo onse olo ataluza chisankho but once ngati unasankhidwapo kukhala MP sudzavutikanso. Amalawi paja timangoyang'anila. Za Amaryllis Hotel zili pati pano

Akati budget is off track ndekuti ndi mbola imeneyo
13/07/2026

Akati budget is off track ndekuti ndi mbola imeneyo

Anthu angokhadzula
13/07/2026

Anthu angokhadzula

Chipere
13/07/2026

Chipere

Zunaid Moti Financed DPP Campaign With US$6 Million, Rewarded With Deals and Appointment as Ambassador-at-LargeMalawi vo...
13/07/2026

Zunaid Moti Financed DPP Campaign With US$6 Million, Rewarded With Deals and Appointment as Ambassador-at-Large

Malawi voice can confidently reveal that South African businessman Zunaid Moti financed the ruling DPP’s election campaign with US$6 million.

According to information available to us Moti’s appointment as Malawi’s Ambassador-at-Large formed part of an agreement under which he would finance the DPP campaign. Following the party’s victory in the September 16 elections, the appointment was subsequently effected.

The letter outlining the terms and conditions of the alleged agreement is dated 12 July 2025, just months before the September 16 elections.We have it in our possession signed by both Moti and Malawi President Mutharika .

In our earlier publication, we revealed that Moti is expected to play a key role in facilitating major investment negotiations involving Malawi’s mining, energy and fuel sectors on behalf of the Government of Malawi.

The reported MK4 billion donation to the First Lady’s BEAM Trust is also cited as part of efforts to strengthen his relationship with the country’s leadership.

We welcome any individual or institution with information that contradicts these claims to come forward with evidence. We maintain that we are in possession of documentation relating to the alleged agreement and remain prepared to substantiate our reporting.

As always, we remain committed to publishing verified facts, ensuring fairness, and giving all parties mentioned an opportunity to respond.

Make a date with us tomorrow as we unpack what is inside the agreement between Malawi government under the DPP leadership and Zunaid Moti .

Address

P. O Box 387
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi voice posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share