25/01/2024
(UTHENGA KWA AZIMAYI )
1. Mamuna aliyense amakonda kwambili chiwelewele kuposa chilichonse... ndinkona amatha kugula chiwelewele olo anthu osauka.... wakabaza olo operekera matope amatha kulipila hule nkulipiraso room banja lake likuvutika chifukwa ndichokoma kwambili kuposaso nsima panyumba....
2. Mamuna ngati ak*tuluka kunja kukanyenga ndek*ti inuyo ngati Mkazi mwatayilira zinthu zambili zokhudzana ndi s*x m'banja mwanumo...
Either munasiya kulilira, mwina munasiya kuyamwa, or munasiya kukisana mwinaso munasiya kunyekulira... k*tayilira azimayi...
3. Mkazi wachibwenzi amadziwa bwino zonse ndikulongosola panozi ndipo iyeyo amalandira ndalama zambili ngati zija munkalandira inu zija muli pachibwezi olo mutangokwatirana kumene chifukwa mamuna wanu ankapeza chomwe amafuna ndicho kunva kukoma pogonana... Mamuna wina aliyense amafewa bwino nthumba ngati akunva kukoma chiwelewele ndipo ndinkona anthu amatha kugulira chibwezi galimo olo kuchimangila nyumba koma mkazi wamnyumba alibe galimoto olo nyumba yake..
4. Akazi ambili okwatira mumalimbikira zinthu zopanda ntchito zaziiii zoti mamuna alibe nazo ntchito.... k*topa ndikuchapa komaso kuphika... izitu sizimakupangani kukhala omusangalatsa mamuna wanu chifukwa zonsezo atha kulemba wantchito olo antchito atatu omamupangila zimenezo. Komatu wantchito sangagwile ntchito yachiwelewele kubedi... moti kumuuza mamuna k*ti lero ndatopa ndichimodzimodzi kumuuza k*ti banjaso ndatopa nalo... Mkazi okonda banja lake chinthu choyamba mutu mwake ndikulingalira k*ti Mulungu anati tiyeni tipange omusangalatsa adamuyu.. kotero ntchito yanu ndikumusangalatsa mamuna wanu basi maka pazomwe zimamusangalatsa mamuna wanuyo (S*X). Pajatu bible limanena k*ti musakanizane. Moti tchimo lokapanga mamuna lachigololo chifukwa choti mukulephera ntchito yanu mnyumba ndilanonse awili tchimoli..
share to 3 groups
Like my page Nankungwi Memory Simwaka
Memorie 2024 Timange Mabanja Angwiro