Ophiri

Ophiri ophiri obonga

28/05/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Step-g Stephano, Blxckie Hezrone KB Mw

Ndalandira phone kuchokela ku likulu ati ndawina kaya chani kaya..mmm university of hard knock life.
25/03/2025

Ndalandira phone kuchokela ku likulu ati ndawina kaya chani kaya..mmm university of hard knock life.

From my inboxAbare ndi alongo tithandizeni m'bale wathu emeneyu sakupezeka mukamuona komwe muliko tiyimbirenipa 09974461...
20/03/2025

From my inbox

Abare ndi alongo tithandizeni m'bale wathu emeneyu sakupezeka mukamuona komwe muliko tiyimbirenipa 0997446128 chonde tithandizeni Zina lake ndi madolo peter

Big shout out to my new rising fans! Pk Mk Innovations
17/02/2025

Big shout out to my new rising fans! Pk Mk Innovations

Luso lilimo ndithu koma chikuchitika apapa ndi chani, kupenta zara, kuvala skirt, kunyada ngati nkazi. Akuluwa anene bwi...
07/02/2025

Luso lilimo ndithu koma chikuchitika apapa ndi chani, kupenta zara, kuvala skirt, kunyada ngati nkazi. Akuluwa anene bwino

31/01/2025

Zina akamanena ngati akuwuza anatu

Ana aja akuti amaposter zonyoza apulo nde apulo aja anawayitanitsa nkuwanyengelera, amvekele, kuti musamandiposite ndikupatseni zingati ana aja amevekele ine ndikufuna ku college wina ndikufuna cash.

2 minutes ana aja akuti ayambilanso ku poster zonyoza kenako apulo kusiya kuwalipira school fees.

Ana aja nkuyipatsa moto!!! A pulo nkuzatulukilanso kuti gayezi tazisiyani izi mukundiyalutsa ana aja gear mpaka 5 apulo ataona kuti ana aja sakumva nkungoyimba phone ku headquarters 2 minutes 1/10 yatulukira.

Zovuta kumvetsa, kalipo kalipo awa akudziwana, why did he decide to reward them with a busary program in the first place? Mmesa inali blackmail. Zinazi chilungamo chake tizakamva kumwamba basi.

Tizinena kuti Eli Njuchi akumanga nyumba osati mansion nyumbayi siinafike pa mansion. Komabe congratulations
30/01/2025

Tizinena kuti Eli Njuchi akumanga nyumba osati mansion nyumbayi siinafike pa mansion. Komabe congratulations

25/01/2025

Mankhwala oti mkazi azingoganiza zaiwe ndi Chan πŸ™„πŸ™„πŸ™„πŸ˜’πŸ˜‰

08/01/2025

Ati oyimba aku Malawi amakondana koma olo mmodzi kubwera poyera kuti akampatse Paul Banda impsyo πŸ˜•

Zimene amakonda JB amazimvesa yekha. Uyu ndi x wake Complex. Sistez ya Phyzo
04/01/2025

Zimene amakonda JB amazimvesa yekha. Uyu ndi x wake Complex. Sistez ya Phyzo

20/12/2024

Does size
really matter?

18/12/2024

HAVING A SISTER IS A BLESSING MENTION HER TO MAKE HER FEEL SPECIALπŸ₯Ίβ€οΈπŸ₯°

Address

Lilongwe

Telephone

+27603370873

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ophiri posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ophiri:

Share