Gunde Media

Gunde Media Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Gunde Media, Media/News Company, Area 36, Lilongwe.

The Leading Marketing and Advertising brand for Events

Services offered at Gunde Media

-Events Marketing advertisements
-Town Storming
-Audio and Video adverts
-Events Equipment
-Ticketing and many more other services

Independence Day Music showKafukufuku akuonetsa kuti This is the Best lineup in 2026 so far..Gunde Media is here to prom...
08/06/2026

Independence Day Music show

Kafukufuku akuonetsa kuti This is the Best lineup in 2026 so far..Gunde Media is here to promote local artists and giving them the Best platform to showcase their talents and unleash their inner beast and build a massive fanbase countrywide!!!!
Providing a chance to upcoming artists to share a stage with bigger acts in the game..

Invite your friends to follow this page for them to follow the unlimited entertainment that GUNDE MEDIA brings at your doorstep 😎

04th July
Wakawaka hotel


HereTostay

Ntchito ndi yomweyi Abale ndi Anzanga tiyeni tikumane pa Waka waka Hotel pa 4 July 🔥🔥🔥
06/06/2026

Ntchito ndi yomweyi Abale ndi Anzanga tiyeni tikumane pa Waka waka Hotel pa 4 July 🔥🔥🔥

The winners are as follows: Bob brageEne RstBoi castol ululuNet work SlimeUSE THE NUMBER BELOW TO GET YOUR TICKETS +265 ...
04/06/2026

The winners are as follows:
Bob brage
Ene Rst
Boi castol ululu
Net work
Slime

USE THE NUMBER BELOW TO GET YOUR TICKETS

+265 985 928 972

Adzanu apeza kale awo
03/06/2026

Adzanu apeza kale awo

kodi akufikani Tagulani ma ticket awiri mutiwonetse mukhala ndi mwayi opata T-shirt imeneyi
03/06/2026

kodi akufikani Tagulani ma ticket awiri mutiwonetse mukhala ndi mwayi opata T-shirt imeneyi

Tiwinitse ma standard ticket lelo kwa anthu 5 omwe ma comment awo akwane 20 likes pofika 21:00 lelo pa 3 June
03/06/2026

Tiwinitse ma standard ticket lelo kwa anthu 5 omwe ma comment awo akwane 20 likes pofika 21:00 lelo pa 3 June

03/06/2026

Guys Show iyi ndani azagone nyumba mmene zima speaker za ku HIFI zimaphizila muja

Ambiri amawona ngati June ndikutali shaaaa... mongokumbutsana ma ticket ama 15k amwezi wa June  ayamba kale kupezeka paj...
01/06/2026

Ambiri amawona ngati June ndikutali shaaaa... mongokumbutsana ma ticket ama 15k amwezi wa June ayamba kale kupezeka paja tsiku la show pakhomo ndi 20k

04th July
Wakawaka hotel
Independence Day Music Show

Kwangotsala ma Hours kuti ma ticket ama 10k achotsedwe mmalo momwe akugulitsidwa,koma musadandaule tiikamoso ena ama 15k...
31/05/2026

Kwangotsala ma Hours kuti ma ticket ama 10k achotsedwe mmalo momwe akugulitsidwa,koma musadandaule tiikamoso ena ama 15k Monday pa 1 June

mongokumbutsana ma ticket ama 10,000 akutha Sunday ndipo pa 1 June tikuyamba ama 15,000 Contact us lero ndi mawa kuti mu...
29/05/2026

mongokumbutsana ma ticket ama 10,000 akutha Sunday ndipo pa 1 June tikuyamba ama 15,000

Contact us lero ndi mawa kuti mupeze ticket yotchipa pamtengo wa 10,000

04th July 2026
Wakawaka hotel

Address

Area 36
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gunde Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share