Yanga-ndi-hit.com

Yanga-ndi-hit.com Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Yanga-ndi-hit.com, Lilongwe.

12/01/2023

BATILE!

12/01/2023

Zimangochitika koma kukanana tikafusirana sizikhala zabwino

11/01/2023

Nthawi inayake kukhala osasa ndibwino you feel relaxed 😌😌

11/01/2023

Ngati zinthu zaDula kulibwino mungosya kugula za easy bas πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ

11/01/2023

Mwadzuka bwanji nose!!!🌞🌞
Koma mwatsuka nkamwa???

  your nothing without me!!!Ayi zikomo a   anzangaπŸ˜”πŸ˜”
10/01/2023

your nothing without me!!!
Ayi zikomo a anzangaπŸ˜”πŸ˜”

Atumbuka 2mins inayake kumakhala serious Guyz izisizoona πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ
10/01/2023

Atumbuka 2mins inayake kumakhala serious
Guyz izisizoona πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ

Apapa nde 2023 wachemaπŸ”₯πŸ”₯Inu a   anzanga ma HIT nde ayambika apapa DOWNLOAD πŸ‘‡πŸ‘‡ muafille nao SevenOmore - Bwinohttps://yan...
10/01/2023

Apapa nde 2023 wachemaπŸ”₯πŸ”₯
Inu a anzanga ma HIT nde ayambika apapa
DOWNLOAD πŸ‘‡πŸ‘‡ muafille nao

SevenOmore - Bwino
https://yanga-ndi-hit.com/sevenomore-bwino-prod-by-sevenomore-yamzybeats/

Quest - Chaka China
https://yanga-ndi-hit.com/quest-chaka-china-prd-by-jeremy/

Sean Morgan - Ndidzagenda
https://yanga-ndi-hit.com/sean-morgan-ndidzagenda-prod-by-cuff-b/

Dannywie X Hypo Danger - Khobiri
https://yanga-ndi-hit.com/dannywie-x-hypo-danger-khobiri-prod-by-dannywie/

Di Da Badder X Vacious - One Man Ah Don
https://yanga-ndi-hit.com/di-dadder-one-man-ah-don-ft-vacious/

Track Cee X Kay Stevoh - My Love
https://yanga-ndi-hit.com/track-cee-x-kay-stevoh-my-love-prod-by-jk-warrior/

Osaiwala kupanga upload ndi K500
WhatsApp/Call (0994175266 / 0888442977)

09/01/2023

Unmarried women please know your status and where you belong:-
18-22 years - Associate Mbeta
23-26 years - Mbeta
27-29 years - Senior Mbeta
30-33 years - Principal Mbeta
34-37 years - Deputy Chief Mbeta
38-40 years - Chief Mbeta
41-48 years - Mbeta General
49 years - Life Moves

Stop laughing just go and get married

Guyz wina asakunamizeni olo mwini wake asakuuzeni boza lankunkhuniza Nkuru Ali mu red jacket PAPA GOPANI ndamene anamupa...
09/01/2023

Guyz wina asakunamizeni olo mwini wake asakuuzeni boza lankunkhuniza
Nkuru Ali mu red jacket PAPA GOPANI ndamene anamupangisa Waxy Kay kusiya kuyimba Coz anamudyere Spotlight.
Ife tapanga kafukufuku ndipo zoona ndizimenezo. Zikomo!!!

GOPAN - TIYENI MY LOVE (Prod By ToniCity MW) (Official Lyric Video)Maenanu mwina simukumava bhobho nanuso mukumayimba zi...
09/01/2023

GOPAN - TIYENI MY LOVE (Prod By ToniCity MW) (Official Lyric Video)

Maenanu mwina simukumava bhobho nanuso mukumayimba zibolobosha kumuposa mwini wake nde verani ndikuwerenga lyric yake tiziimba zofanana coz ayayayi
Stream πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡
https://youtu.be/jJVve04UxDs

09/01/2023

Chinkazi chija chambina yaikulu chija cha looks yabhoo chija timachipopa chija chikamadusa mphongo zose kutcholera khosi chija CHOLERA yachithemulisa uku Shaaa!!!πŸ™†πŸ™†πŸ™† Slay Queen uja apitatu uku

08/01/2023

Papa Gopano - Tiyeni My Love (Prod by Tonicity)πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯
Iyi ndi hit yoti ukangozuka morning automatically ukumangoyamba kuiyimba 😌😌😌
ToniCity MW

Video:https://youtu.be/qzmMqpA_2rs

-Ndi-Hit.comHit.com

08/01/2023

Wa nyonyonyo Pansana pako wava palibe chonwe ungandiuzeπŸ–•πŸ–•πŸ–•

Apa mungapeleke mwambi wanjiA   anzanga!!Nkulu uyu amaba ma drip a Cholera kuchipatala
08/01/2023

Apa mungapeleke mwambi wanji

A anzanga!!
Nkulu uyu amaba ma drip a Cholera kuchipatala

A   tose we should all pay respect to this man here Uyu kudya akazi aeni anali nazo ndi luso Amene amamenyedwa chifukwa ...
08/01/2023

A tose we should all pay respect to this man here
Uyu kudya akazi aeni anali nazo ndi luso
Amene amamenyedwa chifukwa cha nkazi waeni mmodzi akamufuse ma tips kuti zimaenda bwanj pa mpanje pano

Akufuna cross kwa Konkala Official just type TIYENI MY LOOOVE ku comments section
08/01/2023

Akufuna cross kwa Konkala Official just type TIYENI MY LOOOVE ku comments section

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Yanga-ndi-hit.com posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Yanga-ndi-hit.com:

Share