Tiweke Africa

Tiweke Africa African Entertainment Brand,We Advertise Different Businesses. Lets work together as Africa(Tiweke).
(1)

22/09/2025



Wapampando wa bungwe la MEC Annabel Mtalimanja lero wawulutsaso zotsatira zovomelezeka za ma khonsolo okwana 11. Izi zikutanthauza kuti bungweli lawulutsa zotsatira zovomelezeka za makhonsolo 24 mwaonse 36. Zotsatirazi zili motere (mwachidule)

Machinga:
Lazarus Chakwera (MCP) – 4,541
Dalitso Kabambe (UTM) – 2,492
Peter Mutharika (DPP) – 177,387

Nkhotakota:
Lazarus Chakwera (MCP) – 50,776
Dalitso Kabambe (UTM) – 2,866
Peter Mutharika (DPP) – 52,259

Lilongwe City:
Lazarus Chakwera (MCP) – 102,787
Dalitso Kabambe (UTM) – 28,570
Peter Mutharika (DPP) – 145,908

Dowa:
Lazarus Chakwera (MCP) – 216,091
Dalitso Kabambe (UTM) – 3,534
Peter Mutharika (DPP) – 15,906

Chikwawa:
Lazarus Chakwera (MCP) – 7,290
Dalitso Kabambe (UTM) – 2,736
Peter Mutharika (DPP) – 187,283

Nsanje:
Lazarus Chakwera (MCP) – 10,063
Dalitso Kabambe (UTM) – 1,619
Peter Mutharika (DPP) – 93,197

Zomba District:
Lazarus Chakwera (MCP) – 5,676
Dalitso Kabambe (UTM) – 3,761
Peter Mutharika (DPP) – 213,241

Blantyre City:
Lazarus Chakwera (MCP) – 17,419
Dalitso Kabambe (UTM) – 25,572
Peter Mutharika (DPP) – 197,532

Mzimba:
Lazarus Chakwera (MCP) – 91,509
Dalitso Kabambe (UTM) – 19,876
Peter Mutharika (DPP) – 118,117

Balaka:
Lazarus Chakwera (MCP) – 3,343
Dalitso Kabambe (UTM) – 3,389
Peter Mutharika (DPP) – 120,021

Thyolo:
Lazarus Chakwera (MCP) – 2,943
Dalitso Kabambe (UTM) – 2,516
Peter Mutharika (DPP) – 200,131

17/09/2025

MSIPI sizikuoneka bwino.

Pakati pa usiku boma lalengezaso kuti sukulu zitsegulira pa 22 September osati pa 15 ngati m'mene zinamvekera dzulo pa s...
12/09/2025

Pakati pa usiku boma lalengezaso kuti sukulu zitsegulira pa 22 September osati pa 15 ngati m'mene zinamvekera dzulo pa social media.

11/09/2025

UTHENGA OCHOKERA KUBOMA.

Sukulu zikuyamba lolemba likudzali pa 15 September osati pa 22 ngati mene zinalengezedwera pachiyambi.

Akufuna ana a sukulu omwe analembetsa muma sukulu awo akapeze nawo mwayi ovota lachiwiri likudzali.

Address

Lilongwe

Telephone

+265883225226

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tiweke Africa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Tiweke Africa:

Share

Category