Malawi Congress Party

Malawi Congress Party Chipani ndichamoyo ichi.

11/08/2026

Nyamata wa desiel .

Musatekeseke ndi zokamba za anthu omwe sakudziwa za Congress.Ngodya zinayi za Congress. 1 Unity2 Discipline3 Obedient 4 ...
11/08/2026

Musatekeseke ndi zokamba za anthu omwe sakudziwa za Congress.

Ngodya zinayi za Congress.
1 Unity
2 Discipline
3 Obedient
4 Loyalty

HE Dr Lazarus MacCathy Chakwera,the 6th President of the Republic of Malawi wapepesa banja losiidwa la a Banda ndi ndala...
10/08/2026

HE Dr Lazarus MacCathy Chakwera,the 6th President of the Republic of Malawi wapepesa banja losiidwa la a Banda ndi ndalama zokwana K1,000,000.

R.I.P Brian.

๐——๐—ฟ.๐—ง๐—ต๐—ผ๐—บ๐—ฎ๐˜€ ๐—•๐—ถ๐˜€๐—ถ๐—ธ๐—ฎ ๐—ฃ๐—ฎ๐˜†๐˜€ ๐—–๐—ผ๐˜‚๐—ฟ๐˜๐—ฒ๐˜€๐˜† ๐—–๐—ฎ๐—น๐—น ๐—ผ๐—ป ๐—™๐—ผ๐—ฟ๐—บ๐—ฒ๐—ฟ ๐—ฃ๐—ฟ๐—ฒ๐˜€๐—ถ๐—ฑ๐—ฒ๐—ป๐˜ ๐—–๐—ต๐—ฎ๐—ธ๐˜„๐—ฒ๐—ฟ๐—ฎ๐—Ÿ๐—ถ๐—น๐—ผ๐—ป๐—ด๐˜„๐—ฒ,๐— ๐—ฎ๐—น๐—ฎ๐˜„๐—ถHE.Dr. Thomas Bisika today paid a courtes...
10/08/2026

๐——๐—ฟ.๐—ง๐—ต๐—ผ๐—บ๐—ฎ๐˜€ ๐—•๐—ถ๐˜€๐—ถ๐—ธ๐—ฎ ๐—ฃ๐—ฎ๐˜†๐˜€ ๐—–๐—ผ๐˜‚๐—ฟ๐˜๐—ฒ๐˜€๐˜† ๐—–๐—ฎ๐—น๐—น ๐—ผ๐—ป ๐—™๐—ผ๐—ฟ๐—บ๐—ฒ๐—ฟ ๐—ฃ๐—ฟ๐—ฒ๐˜€๐—ถ๐—ฑ๐—ฒ๐—ป๐˜ ๐—–๐—ต๐—ฎ๐—ธ๐˜„๐—ฒ๐—ฟ๐—ฎ

๐—Ÿ๐—ถ๐—น๐—ผ๐—ป๐—ด๐˜„๐—ฒ,๐— ๐—ฎ๐—น๐—ฎ๐˜„๐—ถ

HE.Dr. Thomas Bisika today paid a courtesy call on His Excellency Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, the Former President of the Republic of Malawi. This meeting followed the conclusion of Dr. Bisika's distinguished tenure in London.

During his service, Dr. Bisika held the esteemed position of Malawi High Commissioner to the Court of St. Jamesโ€™s. He utilized this opportunity to express his sincere gratitude to President Chakwera for appointing him to this significant diplomatic role.

Dr. Bisika is widely recognized as one of Malawi's most accomplished diplomats. His exceptional service at the Malawian Embassy in London has been a testament to his dedication and commitment to the nation.

#๐—Ÿ๐—ถ๐—น๐—ผ๐—ป๐—ด๐˜„๐—ฒ๐—Ÿ๐—ถ๐˜ƒ๐—ฒ

๐—›๐—ฎ๐—ฝ๐—ฝ๐˜† ๐—•๐—ถ๐—ฟ๐˜๐—ต๐—ฑ๐—ฎ๐˜† ๐—›๐—ผ๐—ป ๐—๐—ผ๐—ป๐—ฎ๐˜๐—ต๐—ฎ๐—ป ๐— ๐—ณ๐˜‚๐—ป๐—ฒ,๐— ๐—ฃ-๐—Ÿ๐—ถ๐—น๐—ผ๐—ป๐—ด๐˜„๐—ฒ ๐—–๐—ถ๐˜๐˜† ๐——๐—ฒ๐—ฑ๐˜‡๐—ฎ!To the esteemed Hon.Jonathan Kabulanda Mfune,MP for Lilongwe Ci...
10/08/2026

๐—›๐—ฎ๐—ฝ๐—ฝ๐˜† ๐—•๐—ถ๐—ฟ๐˜๐—ต๐—ฑ๐—ฎ๐˜† ๐—›๐—ผ๐—ป ๐—๐—ผ๐—ป๐—ฎ๐˜๐—ต๐—ฎ๐—ป ๐— ๐—ณ๐˜‚๐—ป๐—ฒ,๐— ๐—ฃ-๐—Ÿ๐—ถ๐—น๐—ผ๐—ป๐—ด๐˜„๐—ฒ ๐—–๐—ถ๐˜๐˜† ๐——๐—ฒ๐—ฑ๐˜‡๐—ฎ!

To the esteemed Hon.Jonathan Kabulanda Mfune,MP for Lilongwe City Dzenza constituency: We say Happy Birthday,may your Birthday bloom with the same vibrant dedication you bring to the people of Area 25.

We celebrate your tireless service and wish you a year ahead as radiant and prosperous as your vision for Dzenza.

Happy Birthday Honourable ๐ŸŽ‚๐ŸŽ‚

Press release from His Excellency Dr Lazarus McCarthy Chakwera on the passing of Mr Brian Banda!
09/08/2026

Press release from His Excellency Dr Lazarus McCarthy Chakwera on the passing of Mr Brian Banda!

07/08/2026

Zomwe analankhula President Dr Chakwera dzulo ku maliro a malemu Medrina Muula Ching'oma omwe ndi mayi awo a phungu wa kale olemekezeka a Ezekiel Peter Ching'oma.

Onelani.....

His Excellency Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, Sixth President of the Republic of Malawi and President of the Malawi Cong...
07/08/2026

His Excellency Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, Sixth President of the Republic of Malawi and President of the Malawi Congress Party (MCP).

Mtsogoleri otsutsa mnyumba kunyumba ya malamulo olemekezeka a Simplex Chithyola Banda ati ndi zomvetsa chisoni kuti alim...
07/08/2026

Mtsogoleri otsutsa mnyumba kunyumba ya malamulo olemekezeka a Simplex Chithyola Banda ati ndi zomvetsa chisoni kuti alimi achimanga sakupindula ndi thukuta lawo.

A Chithyola anena izi pa uthenga wawo otsekera mkumano wa nyumba ya malamulo.

A Chithyola ati mitengo yomwe boma linaika pogulitsira chimanga siyikugwilizana ndi zonse zomwe alimi amaika pa ulimi.

Iwo ati kuti mulimi agule thumba la feteleza akumafunika kugulitsa matumba 9 achimanga zomwe ndi zokhumudwitsa.

Pa nkhani ya thumba la chitukuko cha mmadera la CDF, a Chithyola ati ndi zomvetsa chisoni kuti pofika pano palibe khonsolo yomwe yalandira ndalama.

Iwo aonjezera kufotokoza kuti ndi zokhumudwitsa kuti boma lakweza ndalama ya maphunziro ya musukulu za ukachenjede ndi 100 pelesenti kunena kuti boma likuyenera kubweza chiganizo chawo.

Malingana ndi a Chithyola zikanakhala bwino mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika akanachita zokambirana ndi atsogoleri onse omwe analamulira dziko lino kuti akambilane njira zomwe angagwilitse ntchito pothana ndi mavuto omwe a Malawi akukumana nawo.

On 16th August 2026,  will be a day of unveiling the tombstone of our late Hon. Joyce Chitsulo, in the village of Mpeni ...
07/08/2026

On 16th August 2026, will be a day of unveiling the tombstone of our late Hon. Joyce Chitsulo, in the village of Mpeni T/A Govati, Mwanza District.

May Her Soul continue Resting in Peace.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Congress Party posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share