Edidia t

Edidia t singer songwriter 🎹🎹🎸
WhatsApp number 0989465091
[email protected]
Producer

14/08/2026

Nkhani za Masewero pa msika ogula ndi kugulitsana osewera ku Ulaya

🚨 TOTTENHAM IKUFUNA CODY GAKPO! ⚪⏳
Tottenham yayamba zokambirana ndi Liverpool zokhudza Cody Gakpo. Kusamukira kwake kupita ku timu ya Spurs kukuwoneka kuti ndi kotheka. 🇳🇱
ℹ️ Source: Plettigoal

🔴 RASHFORD WABWERERA KU SQUAD YA MAN UNITED!
Marcus Rashford waphatikizidwa mu squad ya osewera 26 a Manchester United pa masewera omaliza a pre-season ndi AC Milan. Akhoza kusewera koyamba Ku Manchester United kuyambira December 2024. 👀
ℹ️ Source: SamC_reports

🚨 NAPOLI IKUFUNA BADIASHILE!
Napoli ikukambirana ndi Chelsea za Benoit Badiashile. Chelsea ikufuna £25M, pomwe Napoli ikufuna mtengo wotsika.
(Source: The Sun Football)

🚨 CHELSEA IKUFUNA ALEX SCOTT NDI ADAM WHARTON!
Chelsea yayambanso kulumikizana ndi Bournemouth pa Alex Scott komanso Crystal Palace pa Adam Wharton. Scott akhoza kugulidwa ndi ndalama zoposa £80M.
(Source: TEAMtalk)

🚨 CHELSEA IKHOZA KUCHEPETSA MTENGO WA MALO GUSTO!
Chelsea ingachepetse mtengo wa Malo Gusto wa £75M ngati Liverpool itawonjezera chidwi chake pa defender wa ku France yi.
(Source: Siphillipssport)

🚨 CHELSEA IKUFUNA JJ GABRIEL WA MAN UNITED!
Chelsea ikufuna kusaina wonderkid wa Man United, JJ Gabriel, yemwe ali ndi zaka 15. United ikukambirana kale contract kuti isunge mnyamatayu, yemwe akufunidwanso ndi matimu akuluakulu ku Europe.
(Source: TEAMtalk)

🚨 COMO YAFUNSA ZA LIAM DELAP!
Como yapanga approach kwa Chelsea zokhudza Liam Delap. Striker-uyu ali pa mndandanda wa osewera omwe Como ikufuna.
(Source: Fabrizio Romano)

🚨 ARSENAL YAGWIRIZANA NDI VINCENT JOSEPH!
Arsenal yagwirizana ndi Liverpool pa osewera wawo wachichepere Vincent Joseph pa kusamukira ku Emirates. Komabe, matimuwa sanagwirizane pa ndalama zolipirira Liverpool.
(Source: The Athletic FC)

🚨 MAN UNITED SIKUFUNA KUGULITSA BRUNO FERNANDES!
Manchester United ilibe cholinga chogulitsa captain wake Bruno Fernandes. Akadali wofunika kwambiri pa mapulani a Michael Carrick ndipo akufuna kupitiriza ku

14/08/2026
ANYAMATA A BOMA NDI LOMWELI ANGATI ANALI KWATHU KUNO AJA  ATI ABA MA BALLOT PAPER KU ZAMBIA.Bungwe loyendesa zisankho nz...
14/08/2026

ANYAMATA A BOMA NDI LOMWELI ANGATI ANALI KWATHU KUNO AJA ATI ABA MA BALLOT PAPER KU ZAMBIA.

Bungwe loyendesa zisankho nziko la Zambia layamba laimisa kae kuwelengera kusatira mkubedwa Kwa ma balot paper ochonga chonga mmadera ena nzikolo

Malingana ndi mareport omwe anamandwa Tv yapeza, nsogoleri otsusa nzikolo a Brian mundubile ndiomwe akusogola ndipo izi zakwiisa anyamata achipani cholamulamula.

Tikubweleserani ma update ena....

Follow zambia

our international artist JOE IKON LOVERS❤️❤️❤️
14/08/2026

our international artist JOE IKON LOVERS❤️❤️❤️

🇪🇸Luis Enrique wati cholinga cha PSG sopano ndi chopambana Champions League kachitatu. 🗣️Enrique palibe timu ku Europe y...
14/08/2026

🇪🇸Luis Enrique wati cholinga cha PSG sopano ndi chopambana Champions League kachitatu.

🗣️Enrique palibe timu ku Europe yomwe ili ndi chidwi chofuna kupambana Champions League pakalipano kuposa PSG.

Zaka ziwiri zapitazo, PSG sinkatengedwa ngati timu yomwe itha kutenga Champions League koma pano zinthu zidasitha.

PSG ikatengaso Champions League idzafanana ndi timu ya Real Madrid yomwe ndi yokhayo mumbiri ya Champions League idakwanitsa kutenga Champions League maulendo atatu otsogozana. Sport

Godfrey Kambewa, mmodzi mwa akuluakulu oyendetsa mpikisano wa ziphadzuwa padziko lonse, wati mphekesera zomwe zikufalira...
14/08/2026

Godfrey Kambewa, mmodzi mwa akuluakulu oyendetsa mpikisano wa ziphadzuwa padziko lonse, wati mphekesera zomwe zikufalira pa malo ochezera kuti Ireen Navicha wataya mwayi wokhala chiphadzuwa chachikulu komanso kuti ali pa nambala 64 mwa 20 apamwamba ndi zabodza. Iye wati anthu asamakhulupirire mphekesera zotere chifukwa sizochokera kwa omwe amayendetsa mpikisano. Pofika pa August 14, mpikisanowu udakali pachiyambi ndipo pali mipikisano ina yambiri yikuchitika monga ya luso, kuphika, kukongola, kuvala ndi chiphadzuwa chokongola mwa cholinga. Kambewa watsindika kuti Malawi ikadalipo mu mpikisanowu ndipo wapempha anthu kuti azidalira uthenga wochokera kwa okonza mpikisanowu.

our goat
14/08/2026

our goat

ukutikazaza
14/08/2026

ukutikazaza

25/07/2026
30/01/2026

Me cooking some thing

Address

Africa
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Edidia t posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Edidia t:

Shortcuts

Share

Category