GOD,S PLAN

GOD,S PLAN Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from GOD,S PLAN, Media, Dowa District Hospital, Lilongwe.

06/07/2022

Ekisodo 20:5 May a Mulungu auk*ti( ndidzalanga ana chifukwa cha Atate awo). Okondedwa nkhani imene Mulungu amamuwuza Mose ndi nkhani imemene anthu timaimva osati mozama kwambiri ayi koma ndi yozama kwambiri.

CHIFUKWA

Izi zik*tanthauza k*ti Ku Chiyuda kwambiri akamati anthu amanena amuna okha ,Okondedwa mukamawelenga pa Ekisodo 14 mupeza k*t amati anthu amene amachoka Ku Aigipto anali anthu 600000 amuna okha okha osaphatikiza akazi
Tamverani amene ndife Manolo timayenela tikhale anthu obadwanso kwatsopano chifukwa Mulungu kudutsila mwaife akupeleka anthu ena amene akhoza kudzatumikilanso dzina la Mulungu. Izi zik*tanthauza k*ti mwana wanu akamwalira inuyo musadatembenuke mtima mwayo akapita Ku chionongeko ,tikunena ana amene asadafike popanga chiganizo okha .Enanso

amati adali oyembekezela pati paja ndikuchoka mbewu imeneyi yukapita kugahena ngati makolo

sadabadwenso kwa tsopano.Ena amati tipemphele chifukwa cha k*ti mwana wanga adafa ndisadatembenuke mtima izi sizoona ayi May a Mulungu amati kwaikika kwa Munthu kufa kamodzi kenako chiweruzilo. Okondedwa tiyeni tikhale ochenjera,tibadwenso kwa tsopano tikapulumuke .Ambuye akudalitseni

sadabadwenso kwa tsop

18/05/2021

1Tim4:1_5Bible likukamba zak*ti Mzimu akunena monenetsa k*ti mmasiku otsiliza ena akudzasokeletsedwa ndikumatsata maphunziro aziwanda.Apa k*tsata maphunziro aziwanda pali njira zingapo (a)Kumapita kwa sing,anga ndikumakhulupilira k*ti mukapezako machilitso ndi maphunziro aziwanda (b)Kumapita kwa anthu ena amene amati ndiopemphera koma ak*ti amagulitsa madzi odalitsa ,kaya ndi anointing oil okondedwa ndik*tsatatu maphunziro a aziwanda.Mach 8 mbiri ya Simon wanyanga ataona achina Petrol k*ti akasanjika dzanja munthu,munthuyo amalandira Mzimu oyera iye adati kumuwuza Petrol k*ti ndikupatsa ndalama k*ti undipatseko k*ti nanenso ndizikachita ngati iwe .Petrol adati ulape k*ti kapena angakikhululukire chimp limeneli chifukwa Mzimu woyera sitimulandira ndi ndalama.Nkhani ya Uzimu siyogulitsana inuyo mumagula komanso ogulitsa muchitazo ndi maphunziro aziwanda Ambuye akudalitseni

Media

CHIFUKWA CHANI LERO lino pamene mau a Mulungu akumveka kwambiri ndipamenenso anthu ochuluka akuchimwanso kwambiri?
18/03/2020

CHIFUKWA CHANI LERO lino pamene mau a Mulungu akumveka kwambiri ndipamenenso anthu ochuluka akuchimwanso kwambiri?

08/01/2020
22/09/2019

Jusus is coming shortly please be prepare1John 5:12

12/09/2019

GOD,S PLAN IS INVITING U

23/08/2019

Genesis 1:26 Bible lik*ti (Ndipo anati Mulungu tipange Munthu mchifanizo cha monga mwa chikhalidwe chanthu alamulire pa nsomba za mnyanja ndi pa mbalame za mlengalenga ndi pa zokwawa pa dziko.Okondedwa tikaona Moyo wanthu wa uzimu ice tikulamulira kapena dziko likulamulira ife?Talingalirani Moyo wanu mbale anthu ochuluka tik*tsatila ma fashion zimene zikuonetsa k*ti dziko lik*tilamulira.Mukudziwa ife tikamwaledzela ndiye k*ti tik*tanthauza k*ti Mulungu amaldzelnso, popeza Bible lik*ti tipange Munthu mchifanizo chanthu monga mwa chikhalidwe chanthu.Mulungu akudzalanga onse onyoza chikhalidwe ndi chfanizo chake,inu amene mukusintha chilengedwe cha Mulungu samalani Gahena awukudikilani ngati simulapa.Inu amend mwaona ngati uhule ndi chikhalidwe samalani Aheberi0:27 Ambuye akudalitseni.

Address

Dowa District Hospital
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when GOD,S PLAN posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category