Abel Boston

Abel Boston Giving untold news

14/06/2025

Akuti ndidya

Today we are cerebrating me... Happy birthday to myself..
17/10/2024

Today we are cerebrating me... Happy birthday to myself..

Ndayesetsa ine ngati Munthu kupirira koma ndikaona momwe tinavutikira kuti prayer house iyi idzuke zandipatsa kulimba mt...
12/10/2024

Ndayesetsa ine ngati Munthu kupirira koma ndikaona momwe tinavutikira kuti prayer house iyi idzuke zandipatsa kulimba mtima, ife ngati community tayesetsa ndithu pamwamba pa mavuto anjala komaso mavuto ena amene tili nawo tayesetsa kumanga mpaka kufika pamenepa,..Iyi ndi mthawira CCAP kuno ku Salima TA kambwiri, ndipo tikufuna thandizo lililonse lomwe lingapezeke kuti tiimalize kuopa ingatigwerenso nthawi yavulayi.. tayesetsa kupanga ma paper sunday komabe sitikufikira pomwe timayenera.. Chifukwa cha mathandizo anu amene mwakhala mukupereka kwa achinyamata komaso anthu ovutika ndinalimbikitsika mkuona kuti thandizo la ine ngati munthu silofunikira pakadali pano koma Mutithandizire kumalizitsa tchalitchi chathuchi Triephornia Thomson Mpinganjira Triephornia Thomson Mpinganjira ...chonde chonde tithandizeni.. ndikukhulupilira uthengawu ukupezani inu monga mlera khungwa.. Lumikizanani nafe pa 0991179620 email [email protected].. Ambuye akudalitseni..

21/06/2024
Salima Tourism Team..... for more you can inbox us [MALAWI]
19/06/2024

Salima Tourism Team..... for more you can inbox us [MALAWI]

if you want them you can link us inbox
07/06/2024

if you want them you can link us inbox

With
09/12/2023

With

23/06/2023

The bible has never said that we won't walk through the darkness but it assured us that God will ease our situations and we will get over it................
Let's keep the faith and praying.

04/06/2023

May every tear that has ever fallen from your tired eyes on my behalf become a river for you in paradise👌

03/06/2023

Imposible is just an opinion....Never stop working💪💪✌

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Abel Boston posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Abel Boston:

Share