Ma nyasa news desk

Ma nyasa news desk Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ma nyasa news desk, Media/News Company, Lilongwe.

BASITU AKUTI NIGERIA YAPANA MA GAY ONSE IYO ZA MATHANYUMA SAKUPANGANAWO😅
31/08/2023

BASITU AKUTI NIGERIA YAPANA MA GAY ONSE IYO ZA MATHANYUMA SAKUPANGANAWO😅

25/08/2023

IWE Extreme Football Club lemekeza Atate wako ndi amako..Usaitelo Silver Strikers FC chabwino ithele draw choncho please😴

28/03/2023

Komatu tangoyamba abale😂

15/03/2023

FULL-TIME ⚽
Bangladesh 1 - 1 Malawi

Ali pheeeeee
15/03/2023

Ali pheeeeee

15/03/2023





75'| Goaal!
Chiukepo Msowoya scores for the Flames

Bangladesh 0-1 Malawi (Chiukepo Msowoya 75')

  HALF TIMEBangladesh 0-0 Malawi
15/03/2023





HALF TIME

Bangladesh 0-0 Malawi

2023 AFCON QualifierTuesday 28th March 2023Malawi vs Egypt  Stadium, 3:00pm1.Standard TicketAdvanceK4000MatchDay K50002....
15/03/2023

2023 AFCON Qualifier

Tuesday 28th March 2023

Malawi vs Egypt Stadium, 3:00pm

1.Standard Ticket
Advance
K4000

MatchDay
K5000

2.VIP Ticket
Advance
K20, 000

MatchDay
K30, 000

Corporate Box
K4000, 000 for 10 people
(No sale on MatchDay)

K670, 000 for 10 people
(with flames Jersey)

Naya oyimba wathu wa zizathela ma penalty  Pearson wakhudzika ndi Cyclone Freddy.....  Achifundo tichitepo kanthu.
15/03/2023

Naya oyimba wathu wa zizathela ma penalty Pearson wakhudzika ndi Cyclone Freddy.....

Achifundo tichitepo kanthu.

Blantyre ku chilimba uku💔
15/03/2023

Blantyre ku chilimba uku💔

 Anthu okwana 11  amwalira pamene anthu ochuluka akusowa m'mudzi wa Ntawuchira kwa mfumu yayikulu Likoswe m'boma la Chir...
15/03/2023



Anthu okwana 11 amwalira
pamene anthu ochuluka akusowa m'mudzi wa Ntawuchira kwa mfumu yayikulu Likoswe m'boma la Chiradzulu mudzi onse utapita ndi madzi dzulo.

Pakadali pano, anthu omwe apulumuka pa ngoziyi akusungidwa pa chipatala cha mission cha Nguludi komanso pa sukulu ya ukachenjede ya Catholic University.

Anthuwa pakadali pano akusamaliridwa ndi mpingo wa katolika ndipo apempha thandizo kwa anthu akufuna kwabwino kuti athandize chifukwa alibe pali ponse pomwe akudalira.

14/03/2023

Anthu oposa 60 amwalira kufikira pano kutsatira Namondwe wa Freddy, ndipo 93 avulala pomwe ena 16 akusowabe.

Namondweyu wakhudza anthu oposa 2115 pomwe nyumba zawo zakokoloka ndi madzi amphamvu mchigawo cha ku m'mwera kwa dziko lino.

Izi ndi malinga ndi nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi.

Pakadali pano nduna yoona za madzi ndi ukhondo Abida Mia akuyendera ena mwa madela omwe akhudzidwawa kuti awone momwe zinthu zilili.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ma nyasa news desk posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share