Montana Platnumz

Montana Platnumz 📱Smartphone tips |🇲🇼MalawiLifestyle|⚽️Football Analyst.

14/08/2026

Mukuziwa kuti camera ya phone yanu anthu ena akugwiritsa nawo ntchito.

13/08/2026

Kodi ungapange bwanji browse pa internet osagwiritsa ntchito data. Wonerani video mpaka kumapeto.

12/08/2026

Malawi the scorcher's inazolowera kuwina 🤣 3 - 1inayo

's

Scorcher's iwina ndi zigoli zochokera kwa Faith Chimzimu
12/08/2026

Scorcher's iwina ndi zigoli zochokera kwa Faith Chimzimu

12/08/2026

Ikani dzina kapena phone number pa lockscreen.

11/08/2026

Ma virus kuchosa mmene mungachosere.

10/08/2026

Mmene mungapangire kuti WhatsApp asamagwiritse ntchito data ngati simunatsegule.

Chinthu ichichi tikutenga 🇲🇼 atinva nyunyunyu.
10/08/2026

Chinthu ichichi tikutenga 🇲🇼 atinva nyunyunyu.

09/08/2026

Kwa amene mukugwira ntchito mu boma, osalimbikira kwambiri pa ntchito po kuti masiku a moyo wako achuluke.
GOOD NIGHT

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Montana Platnumz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share