F.G records

F.G records Recording voice and video shooting.

Nyimbo imeneyo yo tchedwa (Malawi)Link.
21/11/2023

Nyimbo imeneyo yo tchedwa (Malawi)
Link.

Download Malawi by Ephraim Justin ft Ernest mpokosa on Vidmate.com

13/11/2023
11/11/2023

Kwamene akufuna nyimboyake ipite pa YouTube inbox me
0881729386 tivane.

Nduna yowona za maboma ang'ono a Richard Chimwendo wati anthu otchuka atengerepo phunziro pa kuzichepetsa komwe malemu T...
21/10/2023

Nduna yowona za maboma ang'ono a Richard Chimwendo wati anthu otchuka atengerepo phunziro pa kuzichepetsa komwe malemu Thomas Chibade anali nako.

Polankhula m'malo mwa mtsogoleri wa dziko lino a Chimwendo ati chiganizo chomwe anthu a m'mudzi mwa Ngomani anapempha akubanja kuti oyimbayu ayikidwe ku Lilongwe zaonetseratu kuti iye amakhala bwino ndi anthu a mderali.

Malinga ndi a Chimwendo dziko lino lataya mnyamata wa luso kwambiri yemwe nyimbo zake zidali zophunzitsa,kudziwitsa komanso kusangalatsa anthu osiyanasiyana.

Pakadali pano Skeffa Chimoto akusangalatsa anthu omwe asonkhana pa malowa ngati njira imodzi yopereka ulemu otsiriza kwa malemu Chibade.

Akubanja la chibade anenakuti abwela okha kudzatenga thupi lamalemu Thomas chibade,atisalola kuti ayikidwe ku lilongwe.p...
20/10/2023

Akubanja la chibade anenakuti abwela okha kudzatenga thupi lamalemu Thomas chibade,atisalola kuti ayikidwe ku lilongwe.pali kusavana zokhudza komwe ayike malemuyi.

12/10/2023

Kwa oyimba nose ngati mufuna kuti ndikuchotseleni voice pa nyimbo,
Kenaka Inu muyilowe ndi voice yanu,
Zikutheka zimenezo.
Nyimbo iliyose ngati mufuna instrumental
Yokhayo zikumatheka kuno.
Ndi Halen pa Whatsapp
0881729386
Tivanebwinobwino.

Address

Lilongwe

Telephone

+265881729386

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when F.G records posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to F.G records:

Share

Category