Elisha

Elisha MCP Broadcasting and Media Production Company. Chipani Cha Fuko.
(11)

09/08/2026

Adamuchotsapo ntchito ku times chifukwa cha katangale.

09/08/2026

Komano iyeyo mawalo amaliopa?

A Police ya Blantyre, amanga wa police mzawo, sub inspector Brino Kamtepa, kamba kosunga ndalama zokwana K110 million zo...
29/07/2026

A Police ya Blantyre, amanga wa police mzawo, sub inspector Brino Kamtepa, kamba kosunga ndalama zokwana K110 million zomwe mulamu wawo amene amagwira ntchito kwa m'mwenye anaba.

Zapezekanso kuti mulamu wawoyi anawauza a Kamtepa kuti agule galimoto ya mtundu wa Mercedes Benz ndipo ikhale mudzina lawo ndipo a Kamtepa amayendera.

Mulamu wawoyi ataba ndalama zo ku Malawi kuno anachokako kaye.

Amene waululitsa zonse ndi mzawo wa Mulamu wawoyo yemwe deal yokubayi anapanga nawo. A police atamugwira. ndikumutsinatsina ndipomwe anaulura zazimenezi

BAMBO MWALE ALI MU ULULUPolice ya Nkhotakota yamanga Mai Hawa Mafukeni azaka 29 ochokera kwa TA Malengachanzi kamba koko...
29/07/2026

BAMBO MWALE ALI MU ULULU

Police ya Nkhotakota yamanga Mai Hawa Mafukeni azaka 29 ochokera kwa TA Malengachanzi kamba kokoka chida komanso kufinya ma battery mpakana kudula battery limodzi la Bambo Mwale omwe amapanga nawo zogonana.

Mai Mafukeni amapanga business yogulitsa thupi. Ndiye dzulo a Hawa ndi a Mwale anapangana deal ya short time. Mtengo wake K6000.

Ndiye zitatero awiriwa anapita pa lodge ina kukapanga gagaga. A Mwale anapanga round yawo koma anapezeka kuti anena kuti samulipila mzimayiyu chifukwa sanakhalitse round yoyamba yo. Ndiye anapanga round 2. Ndikuyambanso kuchuluka nzeru.

Ndiye Hawa anangowakoka chida kuphatikiza ndi ma battery mpakana Bambo wa anagwa kukomoka. Koma asanakomoke anakuwawa ndi uluru zomwe zinapangitsa eni lodge kufika ku room ku ndikupeza a Mwale ku ma battery ku kukutuluka magazi.

A police anaziwitsidwa. Bambo Mwale kupita nawo pa chipatala Cha boma Cha Nkhotakota, kumeneku ananena kuti nkhani yi, ikufunika chipatala Cha Chikulu Cha Kamuzu Central komwe amwale apititsidwako.

Mai Hawa awatsekela ndipo ayankha mulandu ovulaza munthu3

MUNTHU WA NZERU AMATENGA RESPONSIBILITY PA CHINTHU CHIMENE ADASANKHA YEKHA MOSAKAKAMIZIDWA NDI MUNTHUMUTHARIKA YOU MUST ...
28/07/2026

MUNTHU WA NZERU AMATENGA RESPONSIBILITY PA CHINTHU CHIMENE ADASANKHA YEKHA MOSAKAKAMIZIDWA NDI MUNTHU

MUTHARIKA YOU MUST TAKE RESPONSIBILITY ON JANE ANSAH STRENGTH AND WEAKNESSES AS VICE, MUNAMUSANKHA NOKHA

IMPEACH HER A KU PHWANYA MALAMULO

Mutharika’s Ansah dilemma deepens

During the 2025 election campaign, President Peter Mutharika’s camp branded him the “Ansah” (answer) Malawi needed, but the answer now appears to be facing questions of its own after it emerged that Vice President Jane Ansah was not invited to a Cabinet meeting despite being available.

28/07/2026
27/07/2026

Atelo... 🤣🤣🤣

Koma a Chihana mwasowatu...Nanuso akuikani m'botolo ngati  Aunt Jane?
26/07/2026

Koma a Chihana mwasowatu...

Nanuso akuikani m'botolo ngati Aunt Jane?

Pamene ife kuno tili busy kudwazika matenda athuwa Tanzania ikumanga Jetty yaikulu ku Mbamba bay mu Lake Malawi.Pamene A...
26/07/2026

Pamene ife kuno tili busy kudwazika matenda athuwa Tanzania ikumanga Jetty yaikulu ku Mbamba bay mu Lake Malawi.

Pamene Amalawi tikugona apapa pazichitika business yoospa, Ma container, ma galimoto azichoka ku Mkwera Port imene ili mu Indian ocean, then kukweza ma truck kubweretsa pa Mbamba bay port imene ndi 600 km yokha.

Zikafika pa doko la Mbamba bay ma sitima a TZ azinyamula katundu ndikubweretsa ku Malawi kugwilitsa ntchito lake malawi yomwei.

Of course amalawi azitenga katundu motchipa kwambiri koma Tanzania ipha ma kwacha.

Tanzania is thinking one step ahead of time. Ife as a backward country tili busy kulimbana who should represent Malawi on global stage.


The Savetor Compass

Address

Lilongwe

Telephone

+265996273561

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Elisha posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Elisha:

Shortcuts

Share