15/06/2026
🛑KUVUTIKA NDI MPHAVU AZIBAMBO🛑
Vuto lochepa mphamvu kuchipinda lilipo ndithu. Ndipo vutoli limabwela pa zifukwa zosiyanasiyana ndipo ngati tikufuna kuinjoya nkhani ya ku bed tiyeni zopeweka tizipewe ndikudzitalikira.
ZOYAMBITSA Vutoli:
-Ukulu. Ngati wakula munthu kufika zaka zinazake ngati 50 above automatically mphamvu zimatsika angakhale ena amafika 60 ali still komabe masiku ano ndizovuta ndithu.
-Matenda. Ena si okalamba ayi koma chifukwa cha matenda ena ake omwe ali nawo ngati, sugar, mafuta, magazi etc bas mbali imeneyinso imapotoka ndithu.
-Mankhwala. Ma Chemicals a mmankhwala omwe timamwa nthawi zina amationonga kumbali ya ku Bed komanso.
-Kulela wa azimayi wa kuchipatala. Kulera wa ku chipatala amaononga osati kwa azimayi okha koma kwambiri amationonganso azibambo imafika ndithu nthawi yoti munthu uli bwinobwino koma fwakalala coz of Kulerayu.
-Kulodzedwa, Ma stress, khumudwa Ndi zina zambiri....
REMEDY KUTI mudzikhala ndi mphamvu:
🍀Choyamba mamuna amafunika Kukhala wa fit...azibambo ena ali mma40 ena ma 50 and amadzimva kuti afikapo sangapite kothamanga or kothamangitsa magazi, kotero thupi lawo ndi ma hormones ambiri amagonagona. Mapeto ake umapezeka pang'ono watopa kale, mphindi imodzi yokha nthumadzi kuno...so pofuna kupewa zimenezo limbitsani thupi lanu mudzaona kusintha.
🍀Mphindi 15 or 30 mukukagona tengani dzila kuliswa ndikumwa choncho. Zikalowelerana mthupimo kwa 15to30 ija basi go ahead.
🍀Tengani Cloves ikani mpoto thirani mkaka wa fresh. Ikati pa moto zibwate kenako imwani zili hot 15mints before.
🍀Tengani watermelon ndi nthochi dzitafunani limodzi or mupange Juice mudzimwa mudzaimba lokoma za ku bed.
🍀Mudzipanga ma Exercise a Kegel ndipo ngati mmafooka ku bed za normal osati kudwala or zina, mudzaona kusintha ndi ma Exercise a Kegel.
🍀Tengani Ginger ndi Garlic za fresh, zikanyeni ndipo dziwilitseni madzi akewo amaonjezera mphamvu mthupi komanso kutsuka magazi kukhala abwino ku thupi.
🍀REMEDY YA Strong:
-Tengani half teaspoon ya ma powder awa; Ginger powder, Clove powder, Cinnamon powder, Garlic powder.
Mukadzipeza izi tengani madzi otentha ikani mcup thirani zonsezi then dzipangeni mix bwinobwino dzisiyeni kwa mphindi 5. Kenako tengani Uchi wa original thiranimo teaspoon imodzi. Kenako imwani. Mupange izi kwa one week ndipo Mudzimwa mammawa ulionse musanadye kanthu mmimba muli empty.
Remedy imeneyi imapangitsa magazi kuyenda bwino mthupi ndipo imadzutsa ma hormones komanso imapanga umuna wa thanzi ndi wabwino.
Machiritso amakhala nthawi zonse mmanja mwa Mulungu, mukamva mthupi thamangirani kuchipatala tidziwe vuto lanu.
❓️Nanga inu munali ndi vutoli kapena amuna anu anali ndi vutoli anachira ndi mankhwala anji? Tithandizane.
Osaiwala kuthandiza ena popanga FOLLOW and SHARE. Zikomo
______________________________________________