WE CAN MEDIA GROUP

WE CAN MEDIA GROUP "Voice For The Voiceless"

15/07/2025



Bambo wa zaka 62 Francis Kayuni wazipha poziombera ndi mfuti pa mtima ku Ndilande mu nzinda wa Blantyre.

Malingana ndi mneneri wa polisi ya Ndilande,Chibisa Mulimbika wati malemuwa omwe ndi ochita ntchito za malonda ku Nyambadwe aziombela leroli ku chipinda chawo ndipo mkazi wawo ndi amene anamva kulira kuchokera kuchipindacho.

Iye wati apolisi atafika ku nyumbako anapeza bamboyu ataziombera pa mtima komanso mfuti uli pa k**a yawo yomwe inali ndi mapepala ovomerezeka mu dzina lawo.

Mneneriyu wati zotsatira za chipatala ndi zomwe zatsimikizira za imfa yawo.

Mulimbika wati pakadali pano chifukwa chomwe a Kayuni aziphera okha sichinadziwike ndipo ali mkati mofufuza.

Wolemba: Loyd Kwekwete

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera madzulo ano akhala akuyakhula ku mtundu wa a Malawi.Izitu ndi malingana ndi...
14/07/2025

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera madzulo ano akhala akuyakhula ku mtundu wa a Malawi.

Izitu ndi malingana ndi kalata yomwe yatsikizidwa ndi mlembi kunyumba ya boma Antony Rodgers Kasunda.

Kalatayi yati Dr Chakwera ayankhula kudzera kunyumba yowulutsa mawu ya MBC komanso ndi nyumba zina zowulutsa mawu.

14/07/2025

Petrol explosion claims two lives, leaves one severely burned in Mangochi

A 45-year-old woman and her 13-year-old son have died, while her 20-year-old daughter, Aisha Mussah, sustained severe burns following a fire caused by a petrol explosion that gutted their house on the night of July 13, 2025.

The deceased have been identified as Jika Willard and Sherif Mussah, both from Chiwina Village under Traditional Authority Jalasi in Mangochi.

Reports indicate that the elder son of the deceased, a well-known illegal fuel vendor operating in the Namwera area, had been storing petrol at his parents’ rented house with their consent, despite living elsewhere.

On the night of the incident, the three family members brought a charcoal burner into the house to warm themselves due to cold weather. Unfortunately, the burner was placed too close to the stored fuel, igniting a violent explosion. The resulting fire quickly engulfed the house.

Jika and her son were trapped inside and suffered fatal burns. Their bodies were later recovered, completely burned, with some parts reduced to ashes.

Aisha managed to escape and was rushed to Namwera Rural Hospital, where she was later referred to Mangochi District Hospital for further medical treatment after sustaining burns to both her legs and arms.

The incident was reported to police, who rushed to the scene accompanied by medical personnel. The team confirmed the deaths and retrieved the remains of the victims from the burnt house.

Police in the district have since issued a strong warning to the public to stop illegal fuel vending, emphasizing that such dangerous practices can lead to tragic loss of life and pose serious risks to community safety.

(Inspector Amina Tepani Daudi, Public Relations Officer, Mangochi Police Station)

M'mene zathera lero mu chikho cha NBS National Division League. Wolemba Iqra Adani - Mangochi
13/07/2025

M'mene zathera lero mu chikho cha NBS National Division League.

Wolemba Iqra Adani - Mangochi

FULL-TIME | Malawi 🇲🇼 0 - 3 🇿🇦 South AfricaThe Malawi U-20 national team finishes with 🥈 silver at the AUSC Region 5 You...
13/07/2025

FULL-TIME | Malawi 🇲🇼 0 - 3 🇿🇦 South Africa

The Malawi U-20 national team finishes with 🥈 silver at the AUSC Region 5 Youth Games in Windhoek, Namibia.

A tough loss in the final, but the boys gave it their all throughout the tournament. Proud of the team’s spirit, talent, and hard work! 💪🏾🔥

Source :Malawi National Council of Sports

12/07/2025

Mphunzitsi watimu ya Malawi under 20 Millias Pofera Jengwe wati ali ndi chikhulupiriro masewero a m'mawa ndi timu ya South Africa under 20 timu yake idzachita bwino.

Jengwe wati ndi okondwa kwambiri kuti adapambana pa mwamba pa timu ya Zambia ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi,komanso kubweranso kwa Mofati Mnyotho kwabweretsa chilimbikitso kwa osewera anzake m'masewero a m'mawa kuti timuyi idzachite bwino.

Iye wati anthu dziko muno ayembekezere kuti chikho cha COSAFA Men’s Championship 2025 chibwere ku mudzi kuno.

Wolemba Iqra Adani - Mangochi

Lero pa 12 July 2025 umu ndi m'mene zathera mu NBS National Division League. Wolemba Iqra Adani - Mangochi
12/07/2025

Lero pa 12 July 2025 umu ndi m'mene zathera mu NBS National Division League.

Wolemba Iqra Adani - Mangochi

12/07/2025

SRFA ThumbsUp Premier League

Week 10

Full-time

Saturday 12 July 2025

Chilobwe United 4 - Ntopwa Fc 0

Immigration 2 - Mwanza Stars 1

Fc Thondwe 0 - FCB Nyasa BB Reserve 3

Nsanje United 1- Wanderers Reserve 3

Zingwangwa United 1- Nyambadwe United 1

Wolemba Iqra Adani - Mangochi

Ena mwa masewero omwe alipo lero mu NBS National Division League.Wolemba Iqra Adani - Mangochi
12/07/2025

Ena mwa masewero omwe alipo lero mu NBS National Division League.

Wolemba Iqra Adani - Mangochi

The Malawi U20 National Team has booked a spot in the COSAFA Cup final after a hard-fought 2-1 victory over Zambia in Na...
11/07/2025

The Malawi U20 National Team has booked a spot in the COSAFA Cup final after a hard-fought 2-1 victory over Zambia in Namibia.

A spirited performance sees the junior Flames marching on, sending our neighbors home in dramatic fashion.

Reported by Gift Menlick Tembo- Lilongwe

 .Nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo mdziko muno yalangiza anthu onse ogwilitsa ntchito nyanja za mdziko mu...
11/07/2025

.

Nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo mdziko muno yalangiza anthu onse ogwilitsa ntchito nyanja za mdziko muno Kuti akuyenera kukhalabe osamala kufikira pa nyanjazi patakhala bata.

Langizoli labwela kutsatira ulosi wa momwe nyengo ikhalire usiku uno ndi mawa m’mawa, pomwe yati, anthu ayembekezere nyengo yozizira m’madera ambiri komanso ya chifunga mwapatalipatali koma mvula yowaza igwa m’madera ochepa am’mphepete mwa nyanja ya Malawi kuchigawo cha kumpoto.

Kudzera mukalata yomwe nthambiyi yatulusa yati mphepo iziwomba mochokera kumvuma.

Wolemba Geofrey Friday -Phalombe-

11/07/2025

Police in Mangochi have arrested two men for being found in possession of a live pangolin, a protected species under Malawi's wildlife laws.

According to public relations officer for Mangochi Police Station Inspector Amina Tepani Daudh the suspects have been identified as Andrew Kombo, 33, a Pastor at Malindi Faith Ministries Church, and James Wilson, 55.

The duo were arrested on the evening of July 10, 2025, at Ntagaluka Village, under Traditional Authority Chowe in Mangochi.

Reports indicate that on the said date, Mangochi Police detectives were tipped off by members of the community that two men were in possession of a live pangolin and were offering it for sale.

Acting on the information, police officers, in coordination with officials from the Department of National Parks and Wildlife, rushed to the scene and apprehended the two suspects after they were found with the live pangolin hidden in a black laptop bag.

The suspects will appear before court to answer a charge of illegal possession of specimens of listed species, contrary to Section 110(b) of the National Parks and Wildlife Act, once all documentation is completed.

Police in Mangochi have since warned the public against engaging in the illegal trade of wildlife and have called for continued cooperation in protecting endangered species.

Pastor Kombo hails from Khuyu village, Traditional Authority Mkumba in Likoma while and Wilson comes from Mtiwule Village, Traditional Authority Makanjira in Mangochi.

Reported by Iqra Adani - Mangochi

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when WE CAN MEDIA GROUP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to WE CAN MEDIA GROUP:

Share