Genzoh tv entertainment

Genzoh tv entertainment Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Genzoh tv entertainment, Digital creator, Official page for Ndaziona comedian, Lilongwe.
(2)

18/09/2025
wina number winayo number 9tasankhan number yomwe ikakhale pa mtima wanu lachiwili pano Osaiwara kupanga follow page Gen...
14/09/2025

wina number winayo number 9

tasankhan number yomwe ikakhale pa mtima wanu lachiwili pano Osaiwara kupanga follow page Genzoh tv entertainment

Kodi lachiwiri lino mukachonga pati???APMKabambeChakweraMuluzi Osaiwara kupanga follow page imeneyi Genzoh tv entertainm...
14/09/2025

Kodi lachiwiri lino mukachonga pati???

APM
Kabambe
Chakwera
Muluzi Osaiwara kupanga follow page imeneyi Genzoh tv entertainment

Adadi awa tiyeni tiwavotere Asakhare mokhumata mwava?
13/09/2025

Adadi awa tiyeni tiwavotere
Asakhare mokhumata mwava?

Ndaziona kale amaoneka chonchi pano wafika apa. Genzoh tv entertainment
11/09/2025

Ndaziona kale amaoneka chonchi pano wafika apa. Genzoh tv entertainment

Kwanu ndikuti apa mwina kupeza ma friends achigawo chofanana pa mudzi pano. Osaiwara kupanga follow page Genzoh tv enter...
10/09/2025

Kwanu ndikuti apa mwina kupeza ma friends achigawo chofanana pa mudzi pano. Osaiwara kupanga follow page Genzoh tv entertainment

Chisankho chomaliza pano pa Facebook  16 September 2025 pakati pa awiriwa tivoterepo ndani? Osaiwara kupanga follow page...
09/09/2025

Chisankho chomaliza pano pa Facebook 16 September 2025 pakati pa awiriwa tivoterepo ndani? Osaiwara kupanga follow page iyi Genzoh tv entertainment .

Mwaswera bwanj?
08/09/2025

Mwaswera bwanj?

02/09/2025

1 MCP
2 DPP
3 UTM
Tchula chipani chomwe chimakusangalasa osachita manyazi

Mawa Kwa mwangala kuli msonkhano akuti kubwera mkulu uyu. Koma kuno kwathu palibe chomwe akuchitapo nde tipange bwanji a...
01/09/2025

Mawa Kwa mwangala kuli msonkhano akuti kubwera mkulu uyu. Koma kuno kwathu palibe chomwe akuchitapo nde tipange bwanji azanga ? Sonkhano uchitike kapena ulephere?

Mamuna wina ku Mzuzu wachotsedwa kamwa kamba kopezeka ndi mkaz wa mwini ku Zolozolo,chilango chili pansi pompano😥😥
01/09/2025

Mamuna wina ku Mzuzu wachotsedwa kamwa kamba kopezeka ndi mkaz wa mwini ku Zolozolo,chilango chili pansi pompano😥😥

Driemo watulutsa Bomba lanyimbo link
01/09/2025

Driemo watulutsa Bomba lanyimbo link

Address

Official Page For Ndaziona Comedian
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Genzoh tv entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share