
23/02/2025
Ndiye mwati
Kodi a Onesimus akoma chotani? Kodi mwaimva? Zamalaulotuππ»
Mkadzi wa ku Botswana dzina lake Kessyjan tikunena pano wauyamba ulendo obwera ku Malawi waikwera Ndege akufuna azizamuonela African Chiponde yo pafupi
Phunziro pa nkhaniyi : sitingakulese kuti ubwere koma pomwe wafika Malawi panopa uzathawako wekha zambiri uzazionera komkuno