Kulinso Mbala zoba Nyimbo!! 😅
Koma Mwamva Zoti Adhawawa Kaya Mumati Zonke Kaya ndani Koma Ali pachithuziwa anamubela Nyimbo Mfana Wakumangochi Title 1-0 ... K*tengela ma
Report Akut Mfanayo Akafuna collaboration Ndi Zonke Nde azomke Anamu charger Mfanayo 230k K*t Ayimbe Nawo then Kenako Mfana Uja Anavay studio Kukaika Ma Ma verse ake After azomke Kuimva
Nyimbo ija Basitu Iwo Itemgeni Kajambuliseni Osamuuzaso Mwana Uja ... then Mwana uja Kuzangodabwa Post Pa Mikozi 1-0 to be released Mawa By Zonke... kuyambila Pompo Azomke Sakumuyakhaso Mwana Uja ma foniiii ...
Nyimbo ya Mfanayo Yomwe Ndi yeniyeni Ndi Zonke ndiyiponya Mu comment section mo azonke anachosa ma verse a mwini Nyimbo Kuwaimbaso kawili okha
Side Note : Khalidwe ilili Si labho Sitimgasekelele.. Oimba Otchuka Bwino Bwino Ngat Inu Anthu aziti Mukuba Nyimbo??
13/07/2025
Bwerani mutiuzee zoona, maumboni akumveka kuti nyimbo ijah munachitaa kuba akuluu.
11/07/2025
Chikondi ku Lilongwe wagwesa ina minga
Finally Minga by Chiksy Is out 🔥🔥
LIMITED TICKETS! If you want a good surprise and a deep dive into Praise Umali upcoming album then get your ticket for the intimate listening session scheduled for next weekend Blantyre & Lilongwe . Only limited seats available so get your tickets now cafemaju cocos_at_koa or text the numbers on the flyer.
11/07/2025
Malawi Police Service 😆
11/07/2025
Kindly subscribe to our YouTube Channel
Tangokumana Dropping Soon Same star official & Brightinah 07 :12
Be the first to know and let us send you an email when Just malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.