Charxy Bandry

Charxy Bandry Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Charxy Bandry, Music Producer, Lilongwe.

28/04/2025

Big shout out to my newest top fans! Lika Ancient

05/02/2025
Taonelankoni izi
22/01/2025

Taonelankoni izi

Luso la manja, ngati mukufuna zithunzi zojambulidwa pamanja ndi pensulu ngati chimenechi. Link G Posh Art pa number iyi ...
16/11/2024

Luso la manja, ngati mukufuna zithunzi zojambulidwa pamanja ndi pensulu ngati chimenechi. Link G Posh Art pa number iyi 0987094255.

01/07/2024

One thing about Soldier Lucius Banda kwa ine chomwe ndizamukumbukile nacho, ndichoti, he was the first artist kumuone maso ndi maso ataima pa Jenda (a trading center I grew up). Adatsika mgalimoto yake nkutiyankhula, kutiweva nkutiimbila acapela song yake. Nthawi imeneyi nkuti ndili wachichepele. Ndidasangalara kwambili, chinali chinthu chachilendo komaso chosangalatsa.

01/01/2024

Address

Lilongwe

Telephone

+265884765090

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Charxy Bandry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Charxy Bandry:

Share

Category