Cuff-B

Cuff-B Malawian Recording Producer @ Big Vision Entertainment
Based in Lilongwe Area 49 Dubai African Music Producer from Malawi Lilongwe Area 49 Dubai.
(4)

In the recording  mesa all the way from Bunda.   BIG Vision Entertainment
06/09/2025

In the recording mesa all the way from Bunda.


BIG Vision Entertainment

Yesterday Dancehall inali mkatiMoto unali wambiri mu Booth I had great time creating with the Dancehall Giants Ishan Cya...
05/09/2025

Yesterday Dancehall inali mkati
Moto unali wambiri mu Booth
I had great time creating with the Dancehall Giants Ishan Cyapital & Sean Morgan Official


BIG Vision Entertainment

05/09/2025

Cuff-B wadzuka bho kaya Inu?

04/09/2025

Sikutitu ambirinu simutha koma vuto mumati kuyimba lero kenako psmadutsa chinthawi kuti mudzayimbenso nde choncho simukula ndi music yanu....

Your music requires mature input kuti to grow big kuti audience yanu ikule...

03/09/2025

How would you survive in a world where everyone has the same resources you got,same Skil and access?

Competition is coming and be ready for it. Mukangokhala ndi same mindset yoti tikurana ndife izizi ndipo mudzingoyakabe moto mpaka kale nde muvulala.

We need to upgrade our skills, equipment, software, approach, perception, attitude etc.

Pena kuvutika kuja ndi choice pena chifukwa chakusowa nzeru chabe. Nthawi Zina chifukwa Cha system yomwe inayikidwa ndi anthu okhomelera...

Koma nde zinthu zomwe simungasinthezi muzilora zikuikireni malire? Ati Malawi samamva kulimbikira, sometimes it's how we see things happening and we let them affect us deliberately.

03/09/2025

Money is attracted to Value, increase your value...

Ngati Simukupanga money it might be because of Value....

01/09/2025

Learn saying good things about yourself.
Ati ndine upcoming artist ochepekedwa. Ndine ovutika ,you will be what you believe you are. Manifestation is the key, I will succeed and be great ndipo nyimbo iyiyi iyaka moto.

Cuff-B ndine artist ndimafuna titaweka,ndili ndi nyimbo yomwe I believe will be great ndikaweka ndi iweyo, I have so much faith mundithandiza kukwanilitsa zimenezi.

Kodi ma charges anu amayenda bwanji?

Ma message ngati awa sindingakudyetse blue tick ndipo I like such people okhulupilira ngini yawo ndipo odziwa zomwe akufuna.

Try approach producer winawake or artist yemwe ukufuna kuweka naye with confidence mudzaona response fast fast. Anthuwatu ma message amawapeza koma mumachulutsama ma big ups udyo,thus why they treat you like fans basi.

Ndakuuzirani lero pa 1 Sept 2025
15 days before Voting eti?
Okay...

31/08/2025

Drop YouTube link ya nyimbo yomwe yakuwazani mu recharge Riddim

Copy it and paste it here....

Malinga Mafia Landlord
PQ DDE Tidyerabe
Sangie Forward
Sean Morgan Official Push it
ProVoice Lameck Your Body

Top fan wa anthuwa ayionetse link ya YouTube....

31/08/2025

Audio production ijayo ndiyotchipa Kwathu kuno izizi musazionere pa u ghetto yuti.

Music ili ndi phindu ukaikirapo mtima ndipo zimayenda heavy.
Kulimbikira kuja sikokwanira pali zambiri zomwe mungakonze kuti zanu ziyende.

Image yanu ndiyofunika izikhala ndi chikoka chomupangitsa munthu atamva momwe mumayimbira.

Azimayi amtedza amalawisa nanga Inu anthu nyimbo zanu amazilawa kuti?

Zomangoyika ma video links Anu mumapost a anzanu zija sikuphusha music koma kupu**.
Mukangomuona oteleyo muzirenitu kuti fada wake up.

Zinthu zambiri nzotheka kukonzedwa ndi low budget koma osadzachita chidule ndi Audio yanu Fada. Ndakuuzani lero pa 31st August 2025.

0888414775 mukandifuna mundipeza

I have just finished Recording -B and BLAZE yodellaAnyamata ayionetsa nyimbo eeeh   BIG Vision Entertainment
31/08/2025

I have just finished Recording -B and BLAZE yodella
Anyamata ayionetsa nyimbo eeeh

BIG Vision Entertainment

Address

MALAWI
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Cuff-B posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Cuff-B:

Share

Category