Nyimbo Za Makwaya a Chikatolika

Nyimbo Za Makwaya a Chikatolika Kuphunzitsana matanthauzo a nyimbo zathu

14/09/2026

KWAYA YANU YOKONDEDWA NDIMASALIMO ST.PATRICKS CHOIR MANGOCHI CATHEDRAL IKUBWELANSO NDIMA SALIMO ENA ...
CHOIR YI IKHALA IKULONCHA CHIMBALE CHOMVERA PA 1 NOVEMBER PANO ...ZAMBIRI TIZIKUPATSILANI
Asap ajirikatu

12/09/2026

St maria goretti - st rita chapima ( st marys chemusa )

ST Mary's- ST AnthonyAkhala akubwera pompano..Ndiye paja awa kuimbira Mulungu amakut3nga ngati Business sasewera..Tingod...
10/09/2026

ST Mary's- ST Anthony
Akhala akubwera pompano..
Ndiye paja awa kuimbira Mulungu amakut3nga ngati Business sasewera..
Tingodikira..

10/09/2026

Tiwerenge Bible
Gabriel Mofolo Phiri waikwapula mu chi Rege version..
Monga mwezi wa Bible..

08/09/2026

Mupwetekana pa St Montfort po πŸ˜„πŸ˜„
Sound ili pamenepo tusowa chokamba...

08/09/2026

Zomba Cathedral Choir
Tipatseni yolawa koma asah mukutinzunzatu πŸ˜€πŸ˜€
Tipatseni ipokosere tivine ife.

07/09/2026

St Kizito Catholic Choir Balaka Parish
Koditu anthu mukufatsa..
Izi ndiye zokomazo..

06/09/2026

Tithandizeni ma number abalewa..
Sharpevalle parish

Address

Mitundu Box 175
Lilongwe

Telephone

+27735574000

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyimbo Za Makwaya a Chikatolika posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category