The Malawi Satirical News & Political Parodies

The Malawi Satirical News & Political Parodies Satirical approach to Malawi celebrity news and Politics: The real science of stupid is here Fun

APM tells Manganya to be serious.Running goverment is not drama group.Let's work together and develop this country.APM i...
30/09/2025

APM tells Manganya to be serious.
Running goverment is not drama group.
Let's work together and develop this country.
APM is not mincing words these days.
Kukhadzula basi.

APM fires Norman ChisaleIwe ndathana nawe, ndakulela wakula watha udziwonela wekha kwinako.Watero APM.Zinnka sindikufuna...
30/09/2025

APM fires Norman Chisale
Iwe ndathana nawe, ndakulela wakula watha udziwonela wekha kwinako.
Watero APM.
Zinnka sindikufunanso ata olo pangono.

Pakali pano Chisale mutu suukugwira.
APM has appointed a new Guard from Commander from Neno Police Station and Chisale is jealousy.

Kodi mwini mwini wa DPP ndi ndani?Nanga mayi Calister anathawa atakangana ndi ndani?Bwanji DPP imachita bwino kwambiri n...
30/09/2025

Kodi mwini mwini wa DPP ndi ndani?
Nanga mayi Calister anathawa atakangana ndi ndani?
Bwanji DPP imachita bwino kwambiri nthawi zonse. Nzeru zabwinozi zimachokeka kwandani?
Bingu anamwalila kale kale koma chifukwa chani DPP imachitabe bwino kulibe Bingu?

Tikuyankhani mazulo ano.

Mutharika appoints lady police officer to manage Presidential Traffic ControlSupt Chiphaka
30/09/2025

Mutharika appoints lady police officer to manage Presidential Traffic Control
Supt Chiphaka

Surprise Surprise Surprise!Mutharika dumps Chisale.....appoints a mere Police Officer from Neno Police station AS PRESID...
30/09/2025

Surprise Surprise Surprise!
Mutharika dumps Chisale
.....appoints a mere Police Officer from Neno Police station AS PRESIDENTIAL GUARD COMMANDER

Chisale walira mayo...!
Mutharika alibe kumudzolowela mwachibwana. Amachita zokomela a Malawi ambiri osati munthu modzi ayi.
DPP WOYEE!

Nkhani ya Mchacha siyowona ayi Imvani iziThe truth of the matter has been misrepresented. Hon. Charles Mchacha did not “...
30/09/2025

Nkhani ya Mchacha siyowona ayi
Imvani izi
The truth of the matter has been misrepresented. Hon. Charles Mchacha did not “storm” the offices of the Anti-Corruption Bureau (ACB) as alleged. What actually transpired is far from the picture being painted.

On the said day, Hon. Mchacha went to the ACB premises simply to have his bail signed — a normal legal procedure that he has consistently complied with. As is his practice whenever he is tied up with other duties, he had sent his Personal Assistant (PA) to facilitate the signing. To the surprise of many, the investigator rebuffed the PA and, in an unusual and unprofessional manner, shouted at him.

It was only after being informed of this conduct that Hon. Mchacha personally approached the officer to inquire what the problem was. The exchange that followed was verbal — a conversation that arose out of seeking clarification, not intimidation. At no point did Hon. Mchacha cause fear, panic, or disruption, as is being alleged.

It is therefore misleading to suggest that Hon. Mchacha’s presence amounted to “storming” the offices or threatening the independence of the ACB. What occurred was a misunderstanding blown out of proportion.

Hon. Mchacha remains committed to respecting the rule of law, adhering to due process, and cooperating fully with relevant institutions. Any insinuation to the contrary not only distorts the facts but also risks sowing unnecessary fear and mistrust at a sensitive time for the nation.

Na kuno ku Lilongwe 3trillion inenedwayi hatinayiwone ata.
30/09/2025

Na kuno ku Lilongwe 3trillion inenedwayi hatinayiwone ata.

Mcbride Nkhalamba MCP kachikenanso is possiblemission 2030Join the movement
30/09/2025

Mcbride Nkhalamba
MCP kachikenanso is possible
mission 2030
Join the movement

30/09/2025

Dear Namalomba.
Function iyiyi it was a must attend. This was a biggest function yoti nyumba zoulutsa mawu zakunja zimayenera kupezeka. Pali ma function ena omwe nyumba zoulutsa mawu kapena atolankhani amadikila kuitanidwa koma na iyiyiyi mtolankhani wanzeru amayenera kupitako yekha with or without invitation. APM anayenera kupangitsa msonkhanowu pamalo oti atolankhani ambiri akanakhalapo osati osinila. Msonkhanowu unali wa dziko osati wakubanja kapena chinkhoswe. Dziko lonse lapansi linali tchelu kudikila kuti adadi akhutula chani. Kotero pameyenera kuti nyumba zonse zoulutsa mawu zikanapezekapo. Nthawi zina atolankhani samapezeka pa function kamba kofuna emvulopu yakhaki ayi koma ukulu wankhaniyo. Ndipo iweyo ngati mneneri umayenera kukhala in good relationship with all journalists posatengera komwe amachokera. Chifukwatu nyumba iliyonse yowulutsa mawu imakhala ndi ma listeners ake omwe amafuna azimva zomwe zagwa kunjaku. Kupatula apo, mtolankhani aliyense amakhala ndi angle yake ya story akufuna kulemba based on the media house akuchokera kotero amafuna apezeke pamisonkhano yayikulu ngati iyiyi kuti naye aphaphalitse mafunso mosaopa. Next time, osabwera pa public ndikuyakhula mene watelemu. Izitu zimabweretsa chidani pakati pa atolankhani ndi inu ma organizers or aneneneli.

Tiyeni Tizingokhala Basi

  A Bessie Chirambo atula pansi udindo wawo ngati mlembi oona za kayendetsedwe ka chipani cha People's Development (PDP)...
29/09/2025



A Bessie Chirambo atula pansi udindo wawo ngati mlembi oona za kayendetsedwe ka chipani cha People's Development (PDP) komanso kutuluka chipanichi.

Iwo alembera kalata mlembi wa mkulu wa chipanichi ndipo ndi membala wachitatu kutuluka m'chipanichi kutsatira kutulukanso kwa yemwe anali mkulu owona za achinyamata a Austin Nsopela, Msungichuma a Kennedy Kephas, komanso yemwe anali mkulu owona za ubale wachipanichi ndi mayiko ena, a McDonald Mizati.

Olemba: Thumbiko Nyirongo, Phalombe

kodi mwamva...Nick Chakwera anagula magalimoto 100 cash no discount.Chakwera atawona izi anachita mantha ndipo anamuland...
29/09/2025

kodi mwamva...
Nick Chakwera anagula magalimoto 100 cash no discount.
Chakwera atawona izi anachita mantha ndipo anamulanda kukawasunga.

A MCP apaka bibi ku State House ati APM asalowekoNthambo zamagetsi, ma pipe amadzi akhadzula khadzula.
29/09/2025

A MCP apaka bibi ku State House
ati APM asaloweko
Nthambo zamagetsi, ma pipe amadzi akhadzula khadzula.

Address

Hassan Mwinyi Road
Lilongwe

Telephone

+27619332425

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Malawi Satirical News & Political Parodies posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to The Malawi Satirical News & Political Parodies:

Share