LIWU la MZIKA

LIWU la MZIKA Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from LIWU la MZIKA, Digital creator, Area 47, Lilongwe.

   Mulungu apukute misonzi yanu munyengoyi. Gogo Bika Amwalira ali ndi zaka 101Rest well GOGO.
10/06/2025

Mulungu apukute misonzi yanu munyengoyi.

Gogo Bika Amwalira ali ndi zaka 101
Rest well GOGO.

Lero ndi tsiku lomwe dziko la Malawi tikukumbukira imfa ya anthu 9 omwe anafa pangozi ya ndege ku Nthungwa m`boma la nkh...
10/06/2025

Lero ndi tsiku lomwe dziko la Malawi tikukumbukira imfa ya anthu 9 omwe anafa pangozi ya ndege ku Nthungwa m`boma la nkhatabay. Pangoziyi dziko linataya yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino DR. SAULOS CLAUSE CHILIMA yemwenso anali president wa chipani cha UTM.

Tiyeni tilire nawo akubanja,abwezi komanso abale a onse anatisiya pangoziyi.

Komatu tikudya zinthutu.
21/05/2025

Komatu tikudya zinthutu.

Cholowa sichimaipitsa

Address

Area 47
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LIWU la MZIKA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share