
14/09/2025
Awa ndi ma pictures ama cereb omwe anapezeka ku ukwati wa Piksy ndi mkazi wake Nelly Tembo omwe unachitikira ku Game Haven kwa Bvumbwe.
Mind you! ku reception inali strictly by Invitation mwina nchifukwa kukuoneka anthu ocheperako.