ICheck

ICheck Facts. Verified. Truth. Home Of Creativity

Mchere uja nde akutitu utipha anthufe! Makamaka mziwayamu! Inu mukuona bwa? Si mlingo watsiku limodzi mumasusira chipisi...
03/10/2023

Mchere uja nde akutitu utipha anthufe! Makamaka mziwayamu! Inu mukuona bwa? Si mlingo watsiku limodzi mumasusira chipisi chimodzi chokha kapena nthuli ya nyama imodzi yokha pachiwaya paja?

17/09/2023

Tayandikirani! Nkhani yolemera ija tiimvere limodzi apa.

01/09/2023

Live Launch: Long Acting Injectable HIV PreP

MEC ikuchenjeza za akathyali onama ofuna kubera anthu. Kunja kwaipa. Anthu akumatsegula matsamba amchezo ndicholinga cho...
11/07/2023

MEC ikuchenjeza za akathyali onama ofuna kubera anthu. Kunja kwaipa. Anthu akumatsegula matsamba amchezo ndicholinga chofuna kupeza manambala anu kuti akubereni. Mwazina, amachita izi polengeza za mwayi wa ntchito. Samalani. Zindikirani zachinyengo pa intaneti pano. Falitsani uthengawu.

09/07/2023

Spreaders of seek to abuse your generosity with your attention. Do you know some believe in voice notes they hear on social media without even verification?

Top tips:

1. Don't believe everything in a VN!
2. If it's important, you'll hear it from a credible source!
3. Don't share something whose source you don't know or trust!

▶︎ •၊၊||၊|။||||။၊|။|||။|||။၊|။|||။|||။၊ 05:20

Osazitengeratu. Sizoonayi!
29/06/2023

Osazitengeratu. Sizoonayi!

28/06/2023

🔍 Media Literacy Alert 🔍

Our alert system has drawn our attention to a synthetic/AI generated video circulating on social media depicting a cage fight between tech giants Elon Musk and Mark Zuckerberg.

While it's true that there has been some playful banter between the two about a potential match, the video in question is not real. It's a synthetic media, also known as a deepfake.

Deepfakes use artificial intelligence to create hyper-realistic but entirely fake content. In a world where seeing is usually believing, these videos can blur the line between truth and fiction, potentially spreading misinformation and misleading narratives.

Always remember to verify the source and credibility of what you see online. In the digital age, critical thinking is more important than ever. Stay informed, stay skeptical, and stay safe.

Coming up later this week, the Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) will be hosting an important event in ...
26/06/2023

Coming up later this week, the Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) will be hosting an important event in Lilongwe. The communications regulator will bring together social media influencers from across the country. The purpose of the event is to educate them on the laws governing social media spaces, as well as discussing issues such as fake news and cyberbullying. This is an important meeting and we look forward to keep you informed on the proceedings!

Samalani ndi akathyali - Airtel Yachenjeza!Kampani ya Airtel Malawi yachenjeza kuti pali akuba ena  omwe akufuna kubera ...
19/06/2023

Samalani ndi akathyali - Airtel Yachenjeza!

Kampani ya Airtel Malawi yachenjeza kuti pali akuba ena omwe akufuna kubera anthu pofalitsa mipikisano yachinyengo.

Akubawa akumaika zizindikiro ndi makaka a kampaniyi pamauthenga achinyengo omwe akumafalitsawa.

Chitani izi pofuna kuziteteza kwa achinyengo otere:

1. Musayerekeze kulowa mumpikisano uliwonse musanatsimikize kuti omwe akonza mpikisanowo ndi a kampani yomwe akuti yakonzayo. Chitani izi poyang'ana pa masamba a Facebook, Twitter kapena pa website yawo. Komanso, mverani wailesi chifukwa mipikisano yotereyi amaifalitsanso pa wailesi.

2. Musapereke SIM card, chaunzika kapena zomwe zili pa chitupa chaunzikacho komanso numbala yanu yachinsinsi.

3. Ngati mukafunsidwa kuti mupereke zinthu izi, dziwani kuti ndiakuba. Adziwitseni apolisi komanso a Airtel kuti athane ndi akubawo.

Address

Area 49
Lilongwe

Telephone

+17163207696

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ICheck posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ICheck:

Share