DJ Wadu

DJ Wadu Giving the best not the worst

Anyamata inu zoyenera kupeweka pewani Ngati maganizo ena oyipa akupezani Zitsutseni nokha ndipo musatengeke nawo maganiz...
03/06/2026

Anyamata inu zoyenera kupeweka pewani
Ngati maganizo ena oyipa akupezani
Zitsutseni nokha ndipo musatengeke nawo maganizowo chifukwa amakathera mu siizi

Mnyamata uyu a mmanga zaka zitatu kamba kamaganizo opoira omwen anampeza kti zilako lako zake pa mbuzi

Chikhala amazutsutsa yekha sibwezi zathera mu siizi

20/04/2026

Mwaswera bwanji
Muli bwanji anzanga
kwina kulikonso komwe muli especially my home Village Nkhotakota

Muli bwanji Atsikana ogula zovala zo dhula kwambri kwanu ngakhale bakisngsb kulibe

Sibasi dzuwa linyenga mdima usaka
zeppelin zeppelin zepung

24/01/2026
12/12/2025

Akti waikidwa pa Malo pake

06/08/2024

Wina akuona ngti Airtel yamubwezera ngongole guliramo ma units uwone zomwe ikuchite

01/04/2024

Chibelekelo ft Joseph Nkasa
Pa Channel O
Ngini ilidibho
Mnyamata wa Mchape

Kametedwe kake kameneka Ku Malawi kuno sakhoza kumangoti oba chimanga aja ndamenewa
31/03/2024

Kametedwe kake kameneka
Ku Malawi kuno sakhoza kumangoti oba chimanga aja ndamenewa

Anthu adera amapanga izi
18/03/2024

Anthu adera amapanga izi

22/02/2024

Ambuye tichitileni chifundo
Pamene timalakwitsa muzitikhululukira
Ndife zolengedwa zanu tikupempha mvula osati dzuwa monga zililmu
Tikudziwa kti simulakwidza
Koma tiganizilenkoni 🙏

Mmera wAbwino uja wayamba kunyala 😥😢

Dzina lanu lizamekezedwa munthawi zonse ndi nthawi zosatha

20/02/2024

Kukanika kugona chifukwa chani

Address

Paul Kagame
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ Wadu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category